Chichewa
-
Maudindo ayamba kuchucha m’boma
Pomwe mtsogoleri wa dziko lino yemwe wangosankhidwa kumene Lazarus Chakwera wayamba kusankha adindo m’bom, ku Nyumba ya Malamulo zinthu zasadabuzika.…
Read More » -
Ulimi wa mthirira n’chuma
Tikudziweni… Ndine Moffat Mtalimanja ndipo ndi mkazi wanga Effie timachokera m’mudzi wa Kaunde, ku Namadidi kwa Senior Chief Mlumbe m’boma…
Read More » -
Mthirira usathere panjira
Kaitane Shuga wa m’mudzi mwa a Gavi ku Chileka m’boma la Blantyre ndi mmodzi mwa alimi amene amachita ulimi wothirira…
Read More » -
Chakwera wakwera
Pamene Amalawi amayembekezera bungwe lachisankho kuti lilengeze zotsatira za chisankho cha mtsogoleri wa dziko lino chimene chidachitika Lachiwiri pa 23…
Read More » -
Akhazikitsa kamtengo pachipatala cha nkhalamba
Malingana ndi kuchuluka kwa anthu achikulire amene amabwera pachipatala cha anthu okalamba cha Kalibu Elderly Clinic ku Lirangwe m’boma la…
Read More » -
Takonzeka kuvota—Amalawi
Pamene kwangotsala masiku awiri kuti Amalawi 6.8 miliyoni aponye voti yosankha mtsogoleri wa dziko lino, Amalawi ena asonyeza chidwi kuti…
Read More » -
Atsogoleri akwangula kampeni lero
Migwirizano ya zipani pachisankho chikudzachi zikuomba mkota wa mfundo za kampeni lero ndipo atsogoleri a m’migwirizanoyo akhala ali mbweee! kutolera…
Read More » -
Ampingo avula gule zigoba
Madzi achita katondo kwa Kansonga m’dera la mfumu Chilowoko, m’boma la Ntchisi komwe Akhristu a mpingo wa CCAP wa Biwi…
Read More » -
Phindu lochuluka mu ng’ombe za nyama
Ngakhale ulimi wa ng’ombe za nyama umafuna mpamba wochuluka komanso phindu lake limabwera mochedwa, akadaulo a zaulimi wa ziweto akuti…
Read More » -
Zipani zakonzeka kusankha makomishona
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika wauza zipani za ndale komanso nthambi yoyang’anira ogwira ntchito makhoti (Judicial Service Commission) kuti…
Read More »