Chichewa
-
Kainja wadza ndi lumo lakuthwa
Mkulu wapolisi George Kainja wati adzutsa milandu yonse yogonera n’cholinga chopereka chikhulupiriro mwa Amalawi chokhudza apolisi. Pocheza ndi wailesi ya…
Read More » -
Chisale watuluka n’kumangidwanso
Mawu a wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Klaus Chilima, womwe amauza anthu m’misonkhano yake ya kampeni kuti adzakwizinga…
Read More » -
Sipakala waimitsa Nyumba ya Malamulo
Sipikala waimitsa Nyumba ya Malamulo kwa sabata ziwiri kaamba ka phungu ndi ogwira ntchito ena ku nyumbayi omwe akhudzidwa ndi…
Read More » -
Pa Wenela pasintha zedi
Tsikulo pa Wenela padali fumbi. Lazalo Watsika wabwera ndi moto ndithu. “Abale inu, dzikotu ili limatembenuka zedi. Ndani ankadziwa kuti…
Read More » -
ANatchereza
Sakufuna kukaonekera Gogo Natchereza, Mnyamata wina adandifunsira chibwenzi ndi cholinga choti tidzakwatirane. Padakali pano padutsa zaka zinayi tili paubwenzi, koma…
Read More » -
Tidakumana ku sukulu ku Chiradzulu
Gift Banda ndi mkazi wake Tisunge Mandala adakumana koyamba ali ku sukulu ya sekondale ya Chiradzulu komwe ankaphunzira. Atatsiriza maphunziro…
Read More » -
Bishopu aganiziridwa kugwiririra mwana
Madzi achita katondo pa mpingo wa Assemblies of Fountain ku Chileka m’boma la Lilongwe komwe bishopu wa mpingowu Alexander Selemani…
Read More » -
Chakwera akwanitse malonjezo—HRDC
Bungwe la Human Rights Defenders Coalition (HRDC) lati maso ake akadali otsegula n’cholinga choti boma la Tonse Alliance lisaphwanye ufulu…
Read More » -
Masankhidwe a nduna autsa mapiri pa chigwa
Mtsutso wabuka ndi mmene mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus McCarthy Chakwera, wasankhira nduna za boma lake. Amalawi ena akuti sakuonapo…
Read More » -
Malonjezo ayamba kuoneka
Boma latsopano la Tonse Alliance layamba kukwaniritsa ena mwa malonjezo ake a panyengo ya kampeni ndipo pomwe akadaulo osiyanasiyana ayamikira…
Read More »