Chichewa
-
Mayi akumuganizira Kupha mwana wake
A polisi agwira sing’anga ndi mayi wina powaganizira kuti adapha mwana wa mayiyo wa zaka 11 ku Machinjiri mu mzinda…
Read More » -
Ulima wa chimanga N’kutsatira ulangizi
Katswiri wa zaulimi wa mbewu za m’gulu la masamba ndi zipatso ku Lilongwe University of Agriculture and Natural Resources (Luanar)…
Read More » -
Akhazikitsa lamulo Logonjetsera covid
Boma lakhazikitsa lamulo lothandiza kulimbana ndi mlili wa Covid-19 loti akadaulo azaumoyo akuti ndi chida champhamvu pa nkhondo yolimbana ndi…
Read More » -
Silungwe kufotokoza za lamulo la Covid-19
Boma lakhazikitsa lamulo lomwe cholinga chake ndi kuteteza anthu m’dziko muno ku matenda a Covid-19. STEVEN PEMBAMOYO adacheza ndi woimira…
Read More » -
Akupindula ndi chimanga chachiwisi
Pamene alimi ambiri akugulitsa chimanga chouma pa mtengo wotsika, mlimi wa chimanga chachiwisi ku Area 25 m’boma la Lilongwe Kandida…
Read More » -
Anthu sakudziteteza ku matenda a Covid-19
Ngakhale akadaulo azaumoyo adalosera kuti chiwerengero cha odwala Covid-19 chikwera kwambiri mwezi uno, anthu ambiri sakutsata njira zodzitetezera ku matendawa.…
Read More » -
Chloroquine sachiza Covid-19
Akatswiri azaumoyo atsutsa zoti chloroquine amachiza coronavirus. Akadaulowa amathirirapo ndemanga pa kanema yemwe anthu akugawana pa masamba awo a mchezo…
Read More » -
Ndale zimasokoneza ntchito zathu—MPS
Malawi Police Service (MPS) yavomera kuti mmbuyomu imalephera kugwira ntchito zawo mwaukadaulo kaamba ka andale omwe amalowerera kwambiri pa ntchito…
Read More » -
Fisi wadya mayi wa ku Tsangano
Anthu a m’mudzi mwa Doviko, Mfumu Mpando, m’boma la Ntcheu, akukhala ndi mantha chifukwa cha afisi omwe akuzunguza m’deralo. Loweruka…
Read More » -
Mzomera wadzipereka m’manja mwa apolisi
Gavanala wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) m’chigawo chakumpoto Christopher Mzomera Ngwira wadzipereka m’manja mwa apolisi Lachinayi. Mzomera, yemwe…
Read More »