Chichewa
-
Kwaterera ku DPP
Madzi achita katondo kuchipani cha Democratic Progressive Party (DPP) chomwe chidali m’boma kwa zaka 6 zapitazo ndipo chidagwetsedwa ndi m’gwirizano…
Read More » -
Anatchereza
Ndipite kwa asing’anga? Zikomo Anatchereza, Palitu mkazi amene amandizunguza bongo. Mtima wanga nthawi zonse umakhala pa iye ndipo sindigona tulo…
Read More » -
Njiru yafika pena
Bambo wina wa zaka 30, ali m’chitokosi cha apolisi pomuganizira kuti adapha mwana wake wa zaka 7, ku Chileka mumzinda…
Read More » -
Osangoti neba akuweta nkhumba
Atangomva kuti ulimi wa nkhumba ndi waphindu Leckner Kanyama wa m’boma la Lilongwe adayamba ulimiwu mwansangala poganiza kuti atola chikwama.…
Read More » -
zofunika kulingalira potsegulira sukulu
Miyezi 5 yatha tsopano ana asukulu ali pakhomo chifukwa cha mliri wa Covid-19. Iyi ndi nkhani yomwe yasautsa ndikuyimitsa mitu…
Read More » -
Malingaliro Potsegulira sukulu
Dziko la Malawi latekeseka ndi nkhani yotsegulira sukulu ndipo pofuna kuonetsetsa kuti miyoyo ndi yotetezedwa komanso ufulu wa ophunzira usapitirire…
Read More » -
Nkhumba zimalira chisaliro
Chimodzimodzi ulimi wina ulionse, ulimi wa nkhumba uli ndi ndondomeko yake yoyenera kutsatira poweta kuti mlimi apindule. Mphunzitsi wa zaulimi…
Read More » -
‘Ndinkapita ku ntchito’
John Paul Kayuni ndi mtolankhani panyumba youlutsa mawu ya Zodiak mumzinda wa Lilongwe. Udali m’mawa wa pa April 12, m’chaka…
Read More » -
Kudali ku msonkhano wa mapemphero
Mbusa Willard Maluwa yemwe akutsogolera mpingo wa Fountain of Victory m’boma la Salima adakumana koyamba ndi mkazi wake Abgail Mkwate…
Read More » -
Anatchezera
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza…
Read More »