Chichewa
-
Chakwera wakwera paphiri
Akadaulo osiyanasiyana ati Pulezidenti Lazarus Chakwera waonetsa chamuna popita ku Nyumba ya Malamulo kukayankha mafunso a aphungu pankhani zokhudza dziko…
Read More » -
Anatchereza
Akufuna mwana Gogo, Ndakhala m’banja ndi mwamuna wanga zaka zisanu, koma wopanda mwana. Mwamuna wanga amalimbitsa mtima kuti ndisadandaule popeza…
Read More » -
Kudali ku msonkhano wa mapemphero
Mbusa Willard Maluwa yemwe akutsogolera mpingo wa Fountain of Victory m’boma la Salima adakumana koyamba ndi mkazi wake Abgail Mkwate…
Read More » -
Alimi alirira Admarc
Lipoti la nthambi yochenjeza anthu za njala ya Famine and Early Warning Network (FewsNet) lati alimi a chimanga akupitirira kulira…
Read More » -
Zotsamwitsa pa kutseguliranso sukulu
Pomwe ana asukulu akuyembekezera kutsegulira sukulu, aphunzitsi akuti sadakonzeke zokaphunzitsa chifukwa boma silikuonetsa chidwi pa nkhawa zawo. Mlembi wa bungwe…
Read More » -
Agwiriridwa ali mtulo
Pali zina zikamachitika, sungamvetse kuti zakhala bwanji. Mtsikana wina wa zaka 18 yemwe ali pabanja wagwiriridwa ali mtulo kumalo owedzera…
Read More » -
‘Kudali ku Spar ya ku City Centre’
Beatrice Mushani adakayamba ntchito ku Spar ya ku City Centre mu mzinda wa Lilongwe pa 1 October, 2018. Ndipo udali…
Read More » -
Sandulizani tomato, iphani makwacha
Pamene m’nyengoyi tomato amatsika mtengo chifukwa cha kuchuluka pamsika, katswiri pa luso lopanga zakudya zosiyanasiyana kuchokera ku mbewu za zipatso…
Read More » -
Malingaliro pa malonjezo a Tonse
Boma lolamula la Tonse Alliance lidalonjeza zambiri panyengo ya kampeni. Padutsa miyezi iwiri tsopano kuchoka pomwe mgwirizanowo udalowa m’boma ndipo…
Read More » -
Abwekera tomato wa ufa
Tomato waufa amasungika kwa zaka ziwiri, mtengo wake ndi golide kale komanso ndiwo zake zimakhala za maonekedwe a pamwamba .…
Read More »