Chichewa
-
Aphunzitsi akhala ndi khonsolo
Unduna wa za maphunziro wati ukufuna kukhazikitsa khonsolo ya aphunzitsi yoti izikhazikitsa mwambo komanso kutukula ntchito yauphunzitsi. Nduna ya za…
Read More » -
Akumba manda m’khonde la nyumba
Athu okwiya aika maliro pakhomo pa mkulu wina ku Chirimba mumzinda wa Blantyre yemwe amamanga nyumba panjira yolunjika kuchipata cha…
Read More » -
Aphungu akana makondomu aulere
Aphungu a Nyumba ya Malamulo Lachitatu adabweza mphatso ya makondomu 206 000 yomwe bungwe la Aids Health Foundation (AHF) lidapereka…
Read More » -
Takana kupha makanda
Ife sitivomera kupha makanda.” Uwu ndi uthenga womwe aphungu a Nyumba ya Malamulo auza Tamvani kuti aombera bilo yopatsa mwayi…
Read More » -
182 adzipha mu sept
Chiwerengero cha anthu omwe akudzipha chikunka chikwera m’dziko muno. Kafukufuku amene Msangulutso adapanga akuonetsa kuti sipakutha sabata osamva nkhani kuti…
Read More » -
Akupha makwacha ndi kuchulukitsa mbuzi za chi ‘boer’
Mmalo mopeza K20 000 ku mbuzi yaikulu bwino yachikuda imene imatenga miyezi yosachepera 6 kuti ikule bwino, Allan Kalimasiya wa…
Read More » -
Thirani manyowa mwachangu
Woona za kafukufuku wa za nthaka ku nthambi ya zakafukufuku wa zaulimi ya Bvumbwe m’boma la Thyolo Peter Mfune akuti…
Read More » -
Chakwera, Nankhumwa akhambitsana
Chilinganizo chomwe chidaikidwa pofuna kuti mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera akayankhe mafunso m’Nyumba ya Malamulo chidasanduka mtsutso pakati pa…
Read More » -
Akwapula mphunzitsi wochita ‘chisembwere’
Maphunziro a ana a Sitandade 8, adasokonera Lolemba pasukulu ya pulaimale ya Kalira, yomwe ili m’mudzi mwa Kanyera ku Mtakataka…
Read More » -
Okalamba 46 aphedwa zaufiti
Anthu okalamba 36 adaphedwa pakati pa January ndi December 2019 pomwe ena 10 adaphedwa pakati pa January ndi September 2020…
Read More »