Chichewa
-
Chisankho chizichitika mu September
Aphungu a Nyumba ya Malamulo Lachitatu adavomereza bilo yosintha tsiku la chisankho kuchoka sabata yachitatu ya mwezi wa May kufika…
Read More » -
Uladi akaseweza zaka 5
Khothi lalikulu ku Lilongwe Lachinayi lidagamula mkhalakale pandale Uladi Mussa kuti akasewenze zaka 5 pa mlandu wopotoza dala ntchito ya…
Read More » -
Uladi akaseweza zaka 5
Khothi lalikulu ku Lilongwe Lachinayi lidagamula mkhalakale pandale Uladi Mussa kuti akasewenze zaka 5 pa mlandu wopotoza dala ntchito ya…
Read More » -
‘Kudali ku FDH Bank’
Zina ukamva umakhala kaye jenkha ndi kulingalira kuti kodi makamaka zikuchitikazi ndi zoona kapena ntchedzera chabe. Koma poti suzumile adanka…
Read More » -
Anatchereza
Agogo ndili ndi zibwenzi ziwiri koma onsewo ndi pachibale komanso amadziwana. Ndikawauza kuti andisiye onse amakana, nditani gogo chifukwa onse…
Read More » -
Dzinja ladza, mphenzi zisautse
Anthu akayambana m’madera ena mawu amakhala oti: Tikumana m’dzinja. Uku kumakhala kuopseza kuti akutumizira mphenzi. Kodi n’kotheka kupha wina m’matsenga…
Read More » -
Bajeti yadutsa, koma m’zikhomo
Nyumba ya Malamulo Lachitatu idavomereza bajeti ya K2.2 triliyoni ya chaka cha 2020 mpaka 2021 aphunguwo atayikambirana kuyambira Lolemba. Bajetiyo…
Read More » -
‘Chidodo pamilandu’
Mitima ya Amalawi yayamba kuwira ndi chidodo chomwe chikuchitika pa milandu ina yomwe akadaulo akuti ndi mlingo omwe Amalawiwo akugwiritsa…
Read More » -
Chakwera akumbukira masiku 100 a Tonse
Lolemba, mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera adali ndi mwambo wokumbukira kuti watha masiku 100 akulamula dziko lino. Pamwambo umene…
Read More » -
‘Amalawi dekhani’
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati Amalawi asayembekezere kuti zonse zomwe adalonjeza nthawi ya kampeni zingakwaniritsidwe nyengo yochepa chifukwa…
Read More »