Chichewa
-
MCP ichotsa anthu 30
Chipani cha MCP chachotsa mamembala 30 a chipanichi ku Mzuzu powakaikira kuti amagwirizana ndi mlembi wamkulu wa chipanichi Chris Daza.…
Read More » -
Boma liunikire mfundo zotsatira zionetsero
Kuyankha mfundo 7 zimene anthu adapereka pakutha pa zionetsero zosonyeza kukwiya kwa Amalawi ena ndi mfundo zina za chuma m’boma…
Read More » -
Kaomba adandaula ndi kuchedwa kwa kalembera
Pamene gawo loyamba la ntchito yoti mbadwa za mdziko muno zikhale ndi zikalata za boma yatha, Senior Chief Kaomba ya…
Read More » -
Cama, ma Rasta asemphana pa za zionetsero
Chetechete sautsa nyama zabvumbulukadi kuti pali mangawa aakulu pakati pagulu lotsatira chikhulupiriro cha Chirasta ndi mabungwe omenyera maufulu a anthu…
Read More » -
Fetereza wa makuponi akusowa, atero ena
Pamene alimi ena ali kalikiliki kuthira fetereza wachiwiri m’minda mwawo, Tamvani yapeza kuti fetereza wa makuponi akusowa m’midzi ina ndipo…
Read More » -
Mkangano pakati pa asilamu ndi a gule
Mkokemkoke udakula ku Mitundu mumzinda wa Lilongwe Lamulungu lathali pomwe a gule wamkulu adayamba kukokanakokana ndi anthu a chipembedzo cha…
Read More » -
Cama ikuti zionetsero pa 17
Pamene nkhani yochita zionetsero pokwiya ndi utsogoleri wa Pulezidenti Joyce Banda mmene akuyendetsera dziko lino, ena mwa Amalawi otumikiridwa ati…
Read More »