Nkhani
-
‘Bingu azitsanzika’
Katswiri pa ndale yemwe ndi mphunzitsi wa phunziro la ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, Joseph Chunga wati machokedwe…
Read More » -
Mafumu ku Mwanza akwiya ndi Achewa
Anthu m’midzi ingapo m’boma la Mwanza akunyanyala ntchito zachitukuko pokwiya ndi ganizo la mfumu yayikulu T/A Kanduku loti Achewa m’dera…
Read More » -
Pemphererani dziko lino, ipempha ECM
Mpingo wa katolika wapempha Amalawi kuti apempherere dziko la Malawi ndi utsogoleri wadziko lino panyengo ya Lenti. Muuthenga wake wanyengoyi,…
Read More » -
‘Kunjatidwa kwa Kasambara kunganyanyule mavuto’
Kusamvera mabwalo a milandu komwe boma laonetsa kwasonyeza kulephera kwa chipani cha Democratic Progressive (DPP) pa kulemekeza ufulu wachibadwe, zomwe…
Read More » -
‘Kukonza misewu kukuyenda’
Pali chiyembekezo kuti ntchito za mtengatenga za m’dziko muno zingapite patsogolo chifukwa ntchito zikuluzikulu za chitutuko cha misewu zoposa zisanu…
Read More » -
Mgwedegwede m’zipani wakula
Mgwedegwede womwe wayanga chipani cholamula cha DPP ndi zina zotsutsa boma monga UDF ndi MCP ungabale zisankho zabwino mu 2014,…
Read More » -
Mafumu akhumudwa ndi kuvula amayi
Mafumu komanso anthu m’dziko muno ati ndiokhumudwa ndi zomwe oganiziridwa kuti ndi mavenda m’mizinda wa Lilongwe, Blantyre ndi Mzuzu m’sabatayi…
Read More » -
Akhoti anyanyala ntchito
Mavenda 40 omwe adamangidwa mu mzinda wa Lilongwe sabata yathayi ali m’gulu la anthu zikwizikwi za anthu amene akhudzidwa ndi…
Read More » -
Kuchoka kwa Phoya kutisokoneza, atero ena
Anthu m’madera osiyanasiyana m’sabatayi ati kuchoka kwa phungu wa chipani cholamula cha DPP m’dera la ku m’mawa m’boma la Blantyre,…
Read More » -
Mavuto a UDF angaphe demokalase
Chipasupasu cha m’chipani chakale cholamula cha United Democratic Front (UDF) chingaopseze ulamuliro wa demokalase m’dziko muno womwe umalira kuti pakhale…
Read More » -
Malawi ali pamotoâ€â€Kapito
Mkulu wa bungwe loona ufulu wa ogula la Consumers Association of Malawi (Cama), John Kapito wati boma likuyenera kutulutsa chimanga…
Read More » -
Kasakaniza pa Khrisimasi
Pa 25 Disembala chaka chilichonse Akhristu padziko lapansi amakumbukira kubadwa kwa Yesu. Tsikuli ndi mawa laliwisili. M’malo ambiri m’nyengoyi, chisangalalochi…
Read More »