Category: Chichewa

Gulewamkulu, agumula sitolo

Gulewamkulu wina Lachwiri lapitalo akumukayikira kuti adagumula sitolo ina pamsika wa Nkhalambayasamba m’boma la Mchinji ndipo akumukaikira kuti adasakaza katundu wa K3.5 miliyoni. Mneneri…
Ntchito za wedewede zanyanya

Kusowa ndalama zoyendera zitukuko komanso kulekera anthu a kumudzi kugwira ntchito zomangamanga zachitukuko kukuchititsa kuti ntchitozi zizikhala zawedewede, atero akadaulo ena. Izi zikudza patangotha…
Chilima saima nawo

Uli dere n’kulinga utayenda naye. Amene akufuna kuti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima adzaimire chipanicho pachisankho cha 2019, ati sakutekeseka ndi…
Mswahara wa zifukwa

Munga wadza ndi mafinya omwe. Pamene ena akumwetulira kuti boma lakweza mswahara wa mafumu, mafumu ena ati kukwezaku kuwabweretsera mavuto pa ufumu wawo komanso…
Apayoniya akana zionetsero

Amene adali a Malawi Young Pioneers (MYP) omwe atha miyezi 10 akubindikira ku Lilongwe kufuna ndalama zawo zopumira pantchito ndipo adatsimikiza zokachita nawo zionetserozi…