Chichewa
-
Fisp yabwerera m’bwalo
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika Lachisanu adalengeza kuti ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo yabwerera ku Farm…
Read More » -
Otenga mimba atagwiriridwa akhoza kuichotsa—Bwalo
Mtsikana yemwe adagwiriridwa ali ndi zaka 13 n’kupatsidwa mimba ndi bambo wa zaka 60 m’chaka cha 2022, Lachitatu adati adakhutira…
Read More » -
Zaka 4 chifukwa chosiya mwana yekha
Bwalo la milandu ku Nkhotakota lagamula bambo wa zaka 35 a Anthony Phiri kukakhala ku ndende kwa zaka zinayi popezeka…
Read More » -
Njala saweta, atero kadaulo
Kadaulo pa za malimidwe ndi kuonetsetsa kuti anthu ali nchakudya chokwanira a Tamani Nkhono-Mvula aunikira boma kuti lisamalote pa mpando…
Read More » -
Mpikisano pa usipikala, asankha nduna zina
Pomwe aphungu a Nyumba ya Malamulo ayambe kukumana posakhalitsapa, mpikisano ulipo pofuna kusankha masipikala ngakhalenso aphungu amene akhale m’makomiti. Izi…
Read More » -
Kuteteza chilengedwe
Pomwe vuto la mapulasitiki opyapyala likupitirira kuononga chilengedwe, ophunzira awiri a pa sukulu ya ukachenjede ya Mubas adza ndi mapulasitiki…
Read More » -
Zaka 6 chifukwa choononga njanji
Bwalo la milandu la Second Grade Magistrate m’boma la Dowa lagamula a Laurent Chigowa, a zaka 45 kuti akakhale ku…
Read More » -
Ndikulemba anthu 200—a Mutharika
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika adzudzula anthu omwe akuti amawanena m’masamba a mchezo kuti sadalingalire amayi posankha maudindo…
Read More » -
Amalawi alankhula pa malonjezo
Amalawi ena ati mpofunika ndondomeko zogwirika kuti boma lomwe lalowa kumene la DPP likwaniritse malonjezo ake a m’manifesto. Ena mwa…
Read More » -
Chitonzo chakula
Mmodzi mwa akadaulo a momwe ziwalo za m’thupi zimagwirira ntchito, physiology, wati chiwerengero cha abambo amene amakayezetsa ngati ali obereka…
Read More »