Nkhani
-
Rasta akaseweza zaka 6
Mlandu woba njinga komanso kulasa ndi mpeni paphuzi pa bambo wa kabaza, watumiza Fedson Missi kundende komwe akaseweze zaka 6.…
Read More » -
Malawi ali mu mdima
Zasokonekera! Malawi ali pamoto wosaneneka ndi kuzimazima kwa magetsi. Anthu akumudzi akugona kuchigayo kudikira magetsi pamene alimi a ng’ombe zamkaka…
Read More » -
‘Timakaonera masewero a mpira’
Masewero a pakati pa Police Secondary School ndi St Paul Private Secondary ku Zomba adzakhala chikumbutso kwa Owen Chaima, kuti…
Read More » -
Malawi ali mumdima wa dzaoneni
Dziko la Malawi laona mdima womwe sudaonekepo chilandirireni ufulu wodziyimira palokha. Madera ena akukhala masiku awiri magetsi osayaka. Kwina, ndiye…
Read More » -
Pac iwopseza boma pa bilo yachisankho
Lisafike Lachitatu sabata ya mawa musanabweretse bilo yokhudza chisankho ndi maboma ang’ono. Latero bungwe la amipingo la Public Affairs Committee…
Read More » -
Matafale memorial shows under threat
It is Wednesday. Four days before the annual Evison Matafale Memorial Show in Blantyre. But the Black Missionaries are yet…
Read More » -
Zipani zikufuna mayankho pa zitupa za unzika
Zipani za Malawi Congress Party (MCP) ndi People’s Party (PP) zati kusowa kwa zitupa zina za olembetsa m’kaundula wa unzika…
Read More » -
Zitupa zaunzika zina zasowa
Zitupa 93 893 za uzika m’boma la Kasungu zasowa. Tamvani itha kuvumbulutsa. Izitu zadziwika pamene bungwe lolembera unzika la National…
Read More » -
Achita zionetsero za kuthimathima kwa magetsi
Anthu okhudzidwa a mu mzinda wa Lilongwe adachita ziwonetsero zosonyeza kukwiya kwawo ndi kuthimathima kwa magetsi m’dziko muno. Cholinga cha…
Read More » -
‘Boma likutengera a Malawi kumtoso’
Pamene nkhani ya malamulo oyendetsera zisankho ili mkamwamkamwa, mkulu womenyera ufulu wa anthu, John Kapito, wati nkhani za magetsi, madzi…
Read More »