Nkhani
-
Titsirika nkhalango zonse—Ng’anga
Gulu lina la asing’anga ku Dedza ladzithemba kuti likhoza kuteteza nkhalango za dziko lino ndi chambu koma akuluakulu a boma…
Read More » -
Makuponi n’chipsinjo—Mafumu
Kuchepa kwa makuponi ogulira zipangizo za ulimi zotsika mtengo omwe boma limagawa kwa anthu mogwirizana ndi mafumu, kukubweretsa chitonzo kwa…
Read More » -
Tambala wameza chimanga
Kusadabuzika kwa chipani cha DPP pa chisankho chapadera kukutanthauza kuti Amalawi atopa ndi ulamuliro wa chipanicho, akadaulo a ndale ena…
Read More » -
Za anamapopa sizikuzilala
Nkhani ya anamapopa ikulephera kutha. Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika atangomaliza kuyendera maboma amene anthu angapo aphedwa powaganizira kuti…
Read More » -
Amangidwa popha ‘anamapopa’
Ndende ya Nsanje ikusunga anthu awiri omwe akuyenera kuyankha mlandu wopha Landani Chipira wa zaka 48 atamuganizira kuti ndi ‘namapopa’…
Read More » -
Chipalamba ku Malawi
Dziko la Malawi likusanduka chipalamba. Kafukufuku wathu wapeza kuti mafumu ndi apolisi ena ndiwo akuthandizira kusambula dzikoli pamene akuthandizira kudula…
Read More » -
Bambo amwalira pofuna kulemera
Bambo wina m’boma la Dedza wamwalira atamwa mankhwala oti alemere. “Ukakamwa mankhwalawa, ukafa sabata imodzi. Ukatuluka mphutsi, ndipo akazi awo…
Read More » -
Gule alipo pa 17 October
Zipani za UDF ndi PP zaimika manja kuti sizidzapikisana nawo pamipando ya phungu pachisankho cha chibwereza chimene chikhalepo pa 17…
Read More » -
Pulogalamu ya ECRP yatha
Pulogalamu yophunzitsa anthu kuteteza chilengedwe ya Enhancing Community Resilience Programme (ECRP) yatha itakhalapo zaka 6 ikuphunzitsa anthu m’maboma 7. Mkulu…
Read More » -
Maofesala a kalembera ayera mmanja
Maofesala omwe akugwira ntchito yolembera nzika za dziko lino m’nkalembera wa anthu mwaunyinji ayamba kulandira malipiro awo atsopano. Chiyambireni ntchitoyi…
Read More »