Chichewa
-
Malemia amangidwa zaka 21
Bwalo la majisitileti ku Zomba lachisanu lidagamula Senior Chief Malemia kuti akakhale ku ndende zaka 21 pa mlandu wogonana ndi…
Read More » -
‘Mitengo yomangira ma CDSS yanyanya’
Nduna yoona za maphunziro a Bright Msaka achenjeza kuti ndalama zonse za m’thumba la chitukuko la Constituency Development Fund (CDF)…
Read More » -
Boma lapereka K100biliyoni yogulira chimanga
Nduna ya za chuma, mapulani a za chuma, komanso kupereka mphamvu ku anthu a Joseph Mwanamvekha yati boma lapereka K100…
Read More » -
Chipepeso kaye musanayambe mseu
Nzika zokhudzidwa ku Liwonde m’boma la Machinga zaopsedza kuti ziletsa kuyamba kwa ntchito yokonzanso msewu wa Liwonde-Matawale (M003) pokhapokha boma…
Read More » -
Amanga mayi pa mlandu wovulaza m’nzawo ku nkhope
A Police ku Neno amanga a Grace Samuel a zaka 33 kaamba kowaganizira kuti anavulaza mayi m’nzawo atamuthira madzi otentha…
Read More » -
Mayi wakakamira kuti mlandu wake uwerudzidwe, uthe
Mau aja amati kumayenda kuti uone agalu a michombo adapherezeka mkati mwa sabatayi pomwe mayi wina wa zaka 22 ku…
Read More » -
Aphungu ayembekezere mtsutso wokhetsa thukuta
Pomwe mkumano wa aphungu udayamba Lachiwiri pa 7 July, 2026, nkhani mkati mwa sabatayi zasonyeza kuti mbali yomwe siidakonzekere bwino…
Read More » -
Koma lipoti la hotela ya amaryllis lidzatuluka?
Chikaiko chayambanso kukula ngati lipoti la kafukufuku wa momwe hotela ya Amaryllis idagulitsidwira libwere mu Nyumba ya Malamulo pa mkumano…
Read More » -
Zaka zitatu kwa wogona ndi mbuzi
Bwalo la milandu la First Grade Magistrate la Nkhunga m’boma la Nkhotakota, lagamula a Sandram Lyson, omwe ndi a zaka…
Read More » -
A Mpesi atula pansi udindo
Pomwe kwatsala masiku 30 enieni kuchoka lero kuti chisankho chapadera m’madera angapo chidzachitike, mkulu woyendetsa zisankho ku bungwe la Malawi…
Read More »