Nkhani
-
DPP ikhumudwitsa ku KK
Mafumu ena ku Nkhotakota ndi okwiya ndi chipani cha DPP chimene akuchidzudzula pogwiritsa ntchito galimoto ya chipatala pa ntchito zachipani.…
Read More » -
Njengunje pothana ndi matenda a khansa
Muli ntchito yaikulu m’dziko muno kuti odwala matenda a khansa apeze mpumulo. Izi wanena ndi yemwe adapulumuka ku matendawa, Blandina…
Read More » -
‘Tipulumutseni ku ukwati wa ana’
Amati ana ndi tsogolo la mawa. Koma zikuchitika ku Neno zikukaikitsa ngati adzakhaledi atsogoleri mawa. Kumeneko ukwati wa ana akuti…
Read More » -
Mkangano wa mafumu sukuzirala
Ntchito za chitukuko zagwedera m’boma la Neno, Nsanje komanso Salima kaamba ka mpungwepungwe wa mafumu womwe sukutha. Ku Neno boma…
Read More » -
Apha mkazi ndi apongozi kaamba kothetsa banja
Mnyamata wina wa ku Mangochi wagwa m’manja mwa apolisi atapha mkazi ndi apongozi ake kaamba kothetsa banja. Stephen Sani wa…
Read More » -
Ndende zisanduka makhoti
Zanathina m’mabwalo a milandu. Sitalaka ya ogwira ntchito m’mabwalowa idasandutsa zitokosi za polisi kukhala mabwalo ozengera milandu. Izi zimachitika akuluakulu…
Read More » -
Makhoti ayambanso kugwira ntchito
Sitalaka yomwe ogwira ntchito m’makhoti amachita yatha Lachinayi. Mtsogoleri wa ogwira ntchitowa, Charles Lizigeni, adatsimikizira Tamvani kuti makhoti onse a…
Read More » -
Tidasiya kugwira vakabu—apolisi
Apolisi ati adasiya kugwira vakabu khoti litagamula kuti mchitidwewu umaphwanya ufulu wa anthu. Mneneri wa polisi James Kadadzera watsutsa zomwe…
Read More » -
Chiwerengero cha akaidi chakwera
Chiwerengero cha akaidi m’ndende za m’dziko muno chikunka chikwera. Mmodzi wa akulu owona za ndende m’dziko muno, Masauko Wiscot, wati…
Read More » -
Mavuto a ambulasi anyanya m’zipatala
Ndi Lachiwiri m’mawa. Tili pafupi ndi nyumba yachisoni pachipatala cha Gulupu mu mzinda wa Blantyre. Rose Kaphesi, mwana wake ndi…
Read More »