Nkhani
-
Zili bwino—PAC
Nduna yakale ya zaulimi George Chaponda yamangidwa patatha masiku 43 kuchokera pamene nthumwi kumsonkhano wa Public Affairs Committee (PAC) lidapatsa…
Read More » -
Ziphuphu m’kalembera
Pamene kalembera wa unzika za dziko lino ali mkati, zadziwika kuti anthu ena apeza mpata wosolola m’matumba mwa Amalawi omwe…
Read More » -
Agwira othandiza akunja kupeza zitupa zaunzika
Mmiyezi iwiri yokha chiyambireni kalembera wa zitupa za unzika, Amalawi ena ayamba kugwidwa akuthandiza nzika za mayiko ena kupeza zitupazi.…
Read More » -
Maliro pa chisangalalo
Mwambo wa chikondwerero choti dziko lino latha zaka 53 lili pa ufulu wodzilamurira lidasanduka chisoni pomwe ana 7 ndi bambo…
Read More » -
‘Cashgate’ isokoneza khisimisi kwa a m’boma
Anthu ambiri ogwira ntchito m’boma ali pachiwopsezo chakuti Khisimisi ya chaka chino saiwona bwino chifukwa chosowa ndalama anthu ena ogwira…
Read More » -
MESN ikufuna kuwerengera kwapadera
Mgwirizano wa mabungwe a zachisankho la Malawi Electoral Support Network (Mesn) lati likumenyerera mabungwe ena kuti lidzakhale ndi malo apadera…
Read More » -
Mandela alowa m’manda mawa
Thupi la mtsogoleri woyamba wachikuda wa dziko la South Africa, Nelson Mandela, likuyembekezeka kulowa m’manda mawa kumudzi kwawo ku Qunu…
Read More » -
Mwaulambia alowa m’manda lero
MtThupi la Senior Chief Mwaulambia ya m’boma la Chitipa imene idatisiya Lachiwiri likuyembekezeka kulowa m’manda lero. Mwana wa mfumuyo Briston…
Read More » -
‘JB asabisalire kwa amphawi za kuyenda’
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda wamenyetsa nkhwangwa pamwala ponena kuti, zivute zitani, sangasiye kuyendera anthu m’midzimu ndipo wati zikafika…
Read More » -
Ku Zomba abwekera feteleza wa mbeya
Pa Bungwe la Millennium Villages Projects (MVP) lati nthawi yakwana pamene alimi akuyenera kukolola pogwiritsa ntchito feteleza watsopano wotchedwa Mbeya…
Read More »