Nkhani
-
UDF ingaphe demokalase
Zomwe achita aphungu a chipani cha UDF pokapezeka mbali ya boma m’Nyumba ya Malamulo zingaphe demokalase, watero mphunzitsi wa zandale…
Read More » -
Anthu 50 000 akutenga HIV chaka chilichonse
Pamene nkhondo yolimbana ndi matenda a Edzi ikupitirira, zadziwika kuti chaka chilichonse anthu 50 000 akutenga kachirombo ka HIV kamene…
Read More » -
Kwacha yagwa, valani zilimbe
Anthu akumudzi ati boma lifulumire kuika njira zowatchinjirizira ku zomwe zingadze kaamba ka kugwa kwa ndalama ya kwacha. Anthuwa ati…
Read More » -
Chaka cha anamwino ku Salima lero
Kuli chaka lero ku Salima pamene anamwino m’dziko lino akukondwerera tsiku lokumbukira ntchito yawo pa dziko lapansi. Anamwino padziko lonse…
Read More » -
Bajeti yosadalira ena iphwasuludwa
Kwatha! Ndondomeko ya chuma (bajeti) yosadalira thandizo la maiko akunja ikhadzulidwa, boma latero. Nduna ya zachuma, Ken Lipenga yanena izi…
Read More » -
Mai Banda wati Mafumu asalowe ndale
Mafumu ena a ku Thyolo, Blantyre komanso Chiradzulu akaonekera kale kuchipani cha DPP pamodzi ndi aphungu a Nyumba ya Malamulo…
Read More » -
Phoya amyula maliro aweni, apepesa Achewa
Mkonze mkonze adamyula maliro aweni. Izi mzomwe phungu wa nyumba ya malamulo Henry Phoya anachita msabatayi. Â Imvani izi: mkulu…
Read More » -
‘Aphungu apite m’midzi’
Pomwe sipikala wa nyumba ya malamulo, Henry Chimunthu Banda walengeza Lachitatu m’sabatayi kuti aphungu ayamba kukumana pa 18 Meyi, T/A…
Read More » -
Ma MP olowa PP akonzekere nkhondo
Mphunzitsi wa zandale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College (Chanco), komanso anthu ena ati chipani cholamula cha People’s (PP) chikuyenera…
Read More » -
Amalawi alemekeza Bingu
Amalawi m’zigawo zonse m’dziko muno apereka ulemu wawo wotsiriza kwa yemwe adali mtsogoleri wa dziko lino, Bingu wa Mutharika. Mutharika…
Read More » -
JB asankha Kachali
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda Lachitatu adasankha Khumbo Kachali kukhala wachiwiri wake. Kachali, yemwe ndi phungu wa ku Mzimba,…
Read More » -
Pulezidenti asamale ndi atidye nawo
Mafumu, mphunzitsi wandale kusukulu ya ukachenjede ku Chancellor College kudzanso Amalawi ena ati mchitidwe wa andale ena posintha zipani kuti…
Read More » -
Mikangano yatha
Chisangalalo chadzanso kwa Achewa a m’boma la Mwanza pomwe T/A Kanduku wa m’bomalo walengeza Lolemba pa 26 Malitchi kuti madambwe…
Read More » -
Chikalata cha Sinodi chili ndi mfundo
Boma lisanyozere zounikira za chikalata cha Sinodi ya Nkhoma mu Mpingo wa CCAP younikira mavuto omwe ayanga pakati pa anthu…
Read More » -
Madzi siosewera nawo, maka nthawi yamvula
Madzi ndi moyo, chifukwa amatithandiza m’zambiri. Koma kupanda kusamala, madzi omwewo amadzetsa imfa. Imfa zina za ngozi zamadzi zikhoza kupewedwa.…
Read More » -
Bingu apepese posathetsa mtima pa sitalaka
Pulezidenti Bingu wa Mutharika akuyenera kupepesa Amalawi pa zokhoma zomwe aziona pomwe ogwira ntchito kumabwalo a milandu amanyanyala ntchito. Mkulu…
Read More » -
Kusowa kwa shuga kudzetsa kulira kwa Amalawi
Amalawi m’dziko muno ati sakudziwa chomwe chikuchitika m’dziko muno kotero boma likuyenera kubweretsa mayankho mwachangu zinthu zisadavute. Izi zadza pomwe…
Read More » -
‘Boma lalowa nthenya’
Mphunzitsi kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College, Blessings Chinsinga, wati kumangidwamangidwa kwa anthu omwe akuoneka kuti siabwenzi a boma kukutanthauza…
Read More » -
Boma, mafumu salabadira mavuto a Amalawi
Kusapezeka kwa boma komanso mafumu ku zokambirana zomwe adaitanitsa a bungwe la amipingo la Public Affairs Committee (PAC) sabata yatha…
Read More » -
Kubwera kwa 1 000 Kwacha kukusonyeza sizikuyenda
Kubwera kwa ndalama ya K1 000 yogwirana ndi chisonyezo kuti zinthu sizili bwino pa chuma m’dziko muno, atero akadaulo a…
Read More »