Chichewa
-
Phyzix wadza ndi Captain Long John
Patapita zaka zingapo akutchuka ndi nyimbo zomwe zidavuta monga Cholapitsa, Gamba, Chilombo, Abwana, Memba, Town Monger, Man phyzo, Handsome,…
Read More » -
‘Akwawo ankati Ichocho ndi choopsa’
Ntchito ndi maonekedwe a Yasin ‘Ichocho’ Suwedi, mmodzi mwa akatswiri pankhani yofufumitsa minyewa, ndizo zidali zolepheretsa kuti akwatire Fatima…
Read More » -
Obindikira m’nyumba azengedwa mlandu
Bwalo la milandu la majisitireti mumzinda wa Blantyre lakhazikitsa Lachitatu, 25 May, ngati tsiku lomwe lidzapereke chigamulo kwa banja…
Read More » -
Malamulo Khumi pa Wenela
Tsikulo Moya Pete adadabwitsa tonse. Adafika kumalo otsegulira msonkhano wa ana aja amalimbana za ziii! chaka ndi chaka ati…
Read More » -
Anatchezera
Sakufuna kukayezetsa Anatchereza, Ndakhala ndili pachibwenzi ndi mtsikana wina kwa chaka chimodzi ndipo timakondana kwambiri. Ndine Mkhristu ndipo ndikhulupirira kuti…
Read More » -
Amalawi valani dzilimbe—Mutharika
Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika dzulo watsegulira nkhumano ya aphungu a Nyumba ya Malamulo yokambirana ndondomeko ya…
Read More » -
Mlonda anjatidwa kaamba kosolola
Pamene kampani ya Inovantis m’boma la Machinga imanyadira kuti izigona tulo tozuna chifukwa yalemba ntchito Ibrahim Justin, wa zaka 23,…
Read More » -
Akati ‘tonde azimveka fungo’ akutanthauzanji?
Miyambi ilipo yosiyanasiyana ndipo ina ukaimva mutu umachita kuwira, kulephera kulumikiza mwambiwo ndi tanthauzo lake. Ena amangoti bola ndanenapo mwambi…
Read More » -
Kusowa kwa madzi kusokoneza zambiri ku Lilongwe
Chidziwitso cha Lilongwe Water Board (LWB), bungwe lopopa ndi kugawa madzi mumzinda wa Lilongwe, choti madzi akhala akuvuta kufikira dzinja…
Read More » -
Chipatala chiutsa mapiri pachigwa
Akuluakulu ena a khonsolo ya Lilongwe ndi kontilakitala yemwe akumamanga chipatala cha Biwi mumzinda wa Lilongwe, ayankha mafunso zitadziwika…
Read More » -
‘Adali kasitomala wa mchemwali wanga’
Mchemwali asamangokhala wokuphikira nsima kapena kukuthandiza kuchapa zikavuta, nthawi zina azikhalaso njira yokulondolera njira ya komwe kuli mbali ya…
Read More » -
Wa ku Mangalande anjatidwa atagwiririra wa ku Amerika
Bwalo la Chief Resident Magistrate ku Lilongwe lagamula nzika ya dziko la ku Britain Amrish Magecha kukaseweza zaka 8…
Read More » -
Anatchezera
Ndisathandize mwana wanga? Anatchereza Ine ndi mkazi wanga tidalekana titakhala pabanja zaka ziwiri. Mkaziyu ndidakukwatira titachimwitsana pasukulu ine ndili Fomu…
Read More » -
Asemphana pankhani ya malata, simenti sabuside
Pali kusiyana Chichewa pandondomeko ya malata ndi simenti zotsika mtengo, pamene anthu omwe akuyenera kupindula ndi ndondomekoyi akuti boma tsopano…
Read More » -
Mpando Wamkulu afika pa Wenela
Abale anzanga, tsikulo kudali nyimbo zija zogawa tonse pa Wenela. Adayamba ndi Patience Namadingo, yemwe waimba Nyimbo yotamanda uja mneneri…
Read More » -
Anatchezera
Sagona m’nyumba Anatchereza, Ndili ndi zaka 20 ndipo amuna anga sagona m’nyumba ndiye chonde, ndithandizeni. Akuti ndikawauza ankhonswe banja langa…
Read More » -
‘Idali nthawi ya buleki’
Sukulu iliyonse imakhala ndi nthawi yopumira kapena kuti nthawi ya buleki. Ena amakangosewerako, ena amakadya, koma Paul Chidale ndi…
Read More » -
Boston Kabango: Chikhomo cha Wanderers
Kungomva za Boston Kabango, omwetsa zigoli a matimu ena amayamba kunjenjemera kaamba ka ntchito za mnyamatayu zomwe amazionetsa ku…
Read More » -
Amuganizira kupha apongozi ndi mpeni
Madzi achita katondo m’mudzi mwa Chibwana kwa T/A Mankhambira, m’boma la Nkhata Bay komwe mayi wina wa zaka 27 …
Read More » -
Achita phwando ndi kuimitsidwa kwa Kuluunda
Lero kuli madyerero m’mudzi mwa Senior Chief Bibi Kuluunda m’boma la Salima kusangalalira kuti mfumuyi yaimitsidwa kugwira ntchito yake…
Read More »