Chichewa
-
Milandu ya maalubino Izipita kukhothi lalikulu
Milandu yokhudza kuphedwa kapena kusowetsedwa kwa maalubino tsopano akuti izikakambidwira mukhothi lalikulu lomwe lili ndi mphamvu yopereka chilango chokhwimirapo…
Read More » -
Boma libweza moto pa zolipiritsa m’zipatala
Ganizo la boma loyambitsa mbali yolipiritsa m’zipatala zonse za boma kuyambira July akubwerayu, lalephereka, nduna ya zaumoyo, Peter Kumpalume, yatero.…
Read More » -
Asing’anga akuti akonza zionetsero
Asing’anga m’dziko muno akonza zionetsero zokhumudwa ndi chigamulo cha bwalo lalikulu la Mzuzu chopereka chiletso kuti asiye kugwira ntchito yawo…
Read More » -
Kulakwa, kulakwatu pa Wenela!
Tsikulo lidali lokumbukira asungwana ndi amayi oyendayenda ndipo tidazunguliradi mumzinda wa Lilongwe. Tidali ndi Abiti Patuma kuti ationetse monse.…
Read More » -
Blessings Cheleuka wa pa JOY FM
Amalawi ambiri kuyamba Lolemba mpaka Lachisanu nthawi ya 2 koloko kufika 4 koloko masana amatsegula wailesi ya Joy FM kuti…
Read More » -
Anatchezera
Sakuthandiza Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 21 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Amuna anga adandisiya ataona kuti ndili ndi pathupi…
Read More » -
Mnyamata asiya sukulu chifukwa cha mantha
A makhumbira atakhala msirikali, koma popanda moyo ntchitoyi singatheke. Lero Christopher Robert, mnyamata wachialubino, wasankha kaye moyo posiya sukulu…
Read More » -
Asing’anga asowa mtengo wogwira
Chigamulo cha bwalo lalikulu ku Mzuzu kuletsa asing’anga kuti asagwirenso ntchito m’dziko muno zabweretsa mpungwepungwe ndipo asing’anga eniake akuti…
Read More » -
‘Lidali tsiku la Big Sunday’
Sangwani Mwafulirwa tsopano ndi bambo, si mnyamatanso monga ena akumudziwira chifukwa dzulo pa 4 June 2016 wamulonjeza Trufena Chiwaya,…
Read More » -
‘Timakakonza za ntchito’
Wakaona nyanja adakaona ndi mvuwu zomwe. Mauwa apherezedwa ndi ukwati wa Amos Mazinga wa ku Dowa m’mudzi mwa Ngozi,…
Read More » -
Ntchentchefly zivuta ku Lilongwe
Tsiku limenelo tidakhala pa Wenela ndipo Abiti Patuma adati tipite ku Lilongwe kumenetu ndalama zabooka malinga ndi ungano wa aphungu…
Read More » -
ANATCHEZERA
Wamkulu ndine Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi koma timasiyana ndi chaka chimodzi, wamkulu ndineyo. Kodi tingathe kukwatirana? Iyeyu akufunitsitsa atandikwatira…
Read More » -
Mkangano uimitsa kumanga sukulu
Njovu zikamamenyana umavutika ndi udzu, adatero akulu a mvula zakaale. Izi zapherezeka ntchito yomanga sukulu ya sekondale yoyendera ku…
Read More » -
Henry Mussa: Akusowa tulo ndi Teba
Anthu omwe adagwirako ntchito m’migodi ya m’dziko la South Afrika pamgwirizano wa Temporary Employment Bureau of Africa (Teba) kapena…
Read More » -
Mlonda wosolola ‘solar’ akwidzingidwa
Pamene kampani ya Inovantis m’boma la Machinga imanyadira kuti izigona tulo tabwino chifukwa yalemba ntchito Ibrahim Justin, wa zaka…
Read More » -
Kuweta ng’ombe zamkaka nkokoma, koma….
Alimi ndi akadaulo ena pa zaulimi abwekera ubwino ndi phindu la ulimi wa ng’ombe, koma ati pali zina zoyenera…
Read More » -
Za mafumu m’matuni ndi m’mizinda
Kalata yangayi ndikulemba kubwereza zomwe nthawi ina patsamba lomwe lino ndidadandaulapo zokhudza maufumu a m’mizinda ndi m’matauni. Lero ndabweranso…
Read More » -
Mafupa a alubino si chizimba—sing’anga
Mwadzidzidzi, dziko la Malawi latchuka ndi mbiri yomvetsa chisoni komanso yochititsa manyazi. Iyitu ndi nkhani yozembetsa ndi kupha maalubino ati…
Read More » -
Pezani umuna wa ng’ombe
Nthawi yokhala ndi ng’ombe za makolo yapita. Ndi K1 500 yokha, alimi akhoza kupeza umuna wa ng’ombe za makono.…
Read More » -
kwa Ng’ombe zamkaka zimalira chisamaliro chokwanira
Lasford Mbwana ndi mmodzi mwa alimi a ng’ombe zamkaka omwe akuchita bwino kwambiri kwa Bvumbwe m’boma la Thyolo. Moti mlimiyu…
Read More »