Chichewa
-
‘Mtumiki wa Mulungu adalosera’
Onse okhulupirira amadziwa kuti zodzera m’manja mwa Mulungu n’zodalitsika ndipo zimayenda moyera monga momwe zikuyendera pakati pa mthutha wa…
Read More » -
Kutambasula nthenda ya kadzamkodzo
Kunjaku kuli nthenda zosiyanasiyana koma nthenda zina ukamva, kudulitsa mutu wazizwa. Sabata yapitayi, nduna ya zaumoyo, Dr Peter Kumpalume, adatsogolera…
Read More » -
Ati boma lisabweze ndalama ku FDH
Anthu ena otsata mmene zinthu zikuyendera m’dziko muno aopseza kuti akonza zionetsero ngati boma limvere zonena za banki ya FDH…
Read More » -
Okwiya aimitsa kumanga njanje
Madzi achita katondo ku Nkaya m’boma la Balaka komwe anthu okwiya aletsa kampani ya Mota Engil yomwe ikumanga njanje kumeneko…
Read More » -
Othawa nkhondo akutuwa ndi njala
Kwathina kukampu ya anthu othawa nkhondo m’dziko la Mozambique amene akukhala ku Mwanza ndi Neno komwe anthuwa akutuwa ndi…
Read More » -
‘Mudali m’galimoto ulendo ku Area 23’
Kumwetulira kwa Shreen Mbendera, muulutsi pawailesi ya Galaxy FM, kunachititsa kuti Kimu Kamau amuthere mawu namwaliyu. Ukwati walengezedwa kale…
Read More » -
Zikhulupiriro zina Zisokoneza mdulidwe
Zikhulupiriro zosiyanasiyana zikusokoneza ntchito ya mdulidwe wa abambo womwe unduna wa zaumoyo komanso mabungwe akulimbikitsa, Msangulutso wapeza. Ku Nsanje,…
Read More » -
Aphungu avuta
Tsikulo pa Wenela padali ziii! Moti ojiya, osolola ndi osenza onse adali khumakhuma. Ndalamatu, ndalama zalowa ku silent ndiye…
Read More » -
Tidziwane ndi Enock Balakasi wa Joy Radio
Atolankhani m’dziko muno amakumana ndi zokhoma zambiri makamaka pofuna zoti auze mtundu wa Amalawi. Mwa zifukwa zina, kusoweka kwa lamulo…
Read More » -
Anatchezera
Akufuna mwana Zikomo Gogo, Banja ndi mwamuna wanga lidatha mu 2011. Ndidapeza mwamuna wina yemwe timamvana ndipo tidakayezetsa komwe adatipeza…
Read More » -
Kolondoloza: Mwambo wokaona mwana wa Inkosi
Kumayambiriro kwa chaka chino Angoni ochokera m’boma la Mzimba adali chimwemwe tsaya kaamba ka kubadwa kwa mwana wamwamuna kubanja lachifumu…
Read More » -
Katundu wobwera ku Malawi ali pachiopsezo ku Mozambique
Magulu a zachifwamba m’dziko la Mozambique akuchitira mtopola galimoto zonyamula katundu wosiyanasiyana wobwera m’dziko muno kuchokera kumaiko ena podutsa m’dzikolo.…
Read More » -
Olowa m’dziko mozemba aonjeza mavuto m’ndende
Mavuto a m’ndende za m’dziko muno ngosakamba koma kafukufuku wa Tamvani wasonyeza kuti ena mwa mavutowa akudza kaamba ka anthu…
Read More » -
One-man demo pa Wenela
tsikulo pa wenela padaterera. zidaliko. nkhani idavuta ndi ija tidaiyamba sabata yatha. Inde, iyi nkhani yophana chisawawa, makamaka kwa…
Read More » -
Anatchezera
Anzanga sakundifunsira Ndine mtsikana wa zaka 20, vuto ndili nalo ndi loti sindikufunsiridwa ndi anyamata amsinkhu wanga koma okwatira okhaokha.…
Read More » -
Mike Mkwate: Chilombo pakati pa Bullets
Dzina la Mike Mkwate si lachilendonso m’dziko muno malinga ndi ntchito yomwe akuphika ku Nyasa Big Bullets. Wasewera magemu…
Read More » -
‘Kudali kukwaya ku Mtima Woyera’
Udali ulendo wokhetsa thukuta lowopsa kuti zonse zilongosoke pakati pa Gray Lizimba ndi Iness Chimombo koma zonse zidafika pampondachimera…
Read More » -
Apolisi anjata ‘wolemba ntchito’ apolisi
Pamene Patrick Mayeso Nkhoma wa zaka 28 ndi anzake ena 35 amanyadira kuti ayamba kuzinyambita ndalama za boma akalembedwa…
Read More » -
Milandu ya maalubino Izipita kukhothi lalikulu
Milandu yokhudza kuphedwa kapena kusowetsedwa kwa maalubino tsopano akuti izikakambidwira mukhothi lalikulu lomwe lili ndi mphamvu yopereka chilango chokhwimirapo…
Read More » -
Boma libweza moto pa zolipiritsa m’zipatala
Ganizo la boma loyambitsa mbali yolipiritsa m’zipatala zonse za boma kuyambira July akubwerayu, lalephereka, nduna ya zaumoyo, Peter Kumpalume, yatero.…
Read More »