Chichewa
-
Asintha mlandu wa ‘fisi’
Apolisi Lachinayi adasintha mlandu wa Eric Aniva, amene adamangidwa ataulula kwa mtolankhani wa BBC kuti amagona ndi ana achichepere komanso…
Read More » -
Akuganizira mwana kupha bambo ake
Kudalembedwa m’Baibulo kuti masiku otsiriza mitundu idzaukirana ndipo ana nawo adzaukira makolo awo koma osati momwe zafikira Mponda T/A Nyoka…
Read More » -
‘Idali nthawi ya mapemphero’
Mtsikana akadzakulembera SMS yoti ‘I care for you’ ndiye kuti zatheka chifukwa uthengawu ndi waukulu kwambiri. Zidayambanso choncho ndi Alison…
Read More » -
Apempha mafumu kuunika miyambo
Boma komanso nthambi ya mgwirizano wamaiko wa European Union (EU) atsindika kufunika koti mafumu aunikenso miyambo ina yomwe ikadatsatidwa m’zigawo…
Read More » -
Kuvulaza namfedwa
Ndinali pa maliro ena masiku apitawa komwe amfumu adaganiza zokhutula nkhawa zawo za anamfedwa tili kumanda. Amfumuwo adati sadakondwe…
Read More » -
MOYO UKUTHINA
Amalawi ena ati mavuto ankitsa ndipo akusowa mtengo wogwira pamene akadaulo a zachuma akuti mavutowa afikanso pena chifukwa cha…
Read More » -
Kutambasula unamwali wa mtete
Nyazgambo kuonetsa momwe ankavinira Ndakupezani kuno ku Embangweni. Tatiuzeni zambiri za mtete. Mtete ndi unamwali womwe kalelo ankatilangira. Ankatitsekera…
Read More » -
Maule akusambabe wamkaka
Khomo la ukwati silisowa. M’banja la Nyasa Big Bullets kudakali chisangalalo kutsatira chipambano chawo pobabata asilikali a ku Mzuzu,…
Read More » -
Kuikira kumbuyo khalidwe loipa
Zimanenedwanenedwa zinthu ngati izi kwa amayi okwatiwa: “Osamasiyira Anaphiri kuti azingophikira abambo, kenaka akulandani banja…” “Osaleka kudzisamalira chifukwa bamboyo…
Read More » -
Taphulanji m’zaka 52?
Anthu komanso atsogoleri ena ati zaka 52 za ufulu wodzilamulira zomwe dziko la Malawi lidakwanitsa Lachitatu ndi nthabwala chabe…
Read More » -
Anatchezera
Akundimana Anatchereza, Ndakhala pabanja ndi mkazi wanga kuyambira mu 2011. Poyamba zonse zimayenda koma masiku ano ndikamufuna masiku ambiri amanena…
Read More » -
‘Ndinkafuna mkazi wamakhalidwe’
Ronald Mwandama amene amakhala m’dera la Bangwe ku Blantyre adakhala zaka ziwiri wopanda wapambali atamwalira mkazi wake. Mu 2014…
Read More » -
Asemphana maganizo Pa ulimi wa ‘chamba’
Alimi ambiri m’dziko muno ati ndi okonzeka kuyamba kulima ‘chamba’ chosazunguza ubongo mmalo mwa fodya bola boma liwaunikire zomwe…
Read More » -
Tame Mwawa: Phwete ndiye kudya kwake
Sewero la Tikuferanji ndi limodzi mwa masewero omwe amapereka phunziro kwa anthu pazochitika m’moyo wa tsiku ndi tsiku komanso…
Read More » -
Msika wa ziwala, mbewa
Tidali pamalo aja timakonda pa Wenela, mnyamata uja Bonny Wasawaliya Kanindo atafika ku nyumba ya ulemu ku Nyumba ya…
Read More » -
Kodi Chipuwa wabwerera kumalonda?
Luso la Richard Chipuwa, goloboyi wa Flames komanso Mighty Be Forward Wanderers ndi losayamba. Pa 15 January chaka chino…
Read More » -
Zovula pa Wenela ayi, tamva!
Tsikulo pa Wenela padali ziii! Moti ojiya, osolola ndi osenza onse adali khumakhuma. Ndalamatu ndalama zalowa ku silent ndiye…
Read More » -
Kalindo walasa!
Akulu akale adati kulasa mtengo nchamuna chomwe. Makono tikhoza kunena kuti kuyenda pamsewu utavala ‘mwado’ n’kuvula komwe! Ndawala ya…
Read More » -
Chilango cha kunyonga chiutsa mapiri pachigwa
Ndawala yofuna kubwezeretsa chilango choti wopha mnzake naye aphedwe yavumbulutsa maganizo osiyanasiyana pakati pa mafumu, anthu ndi boma. Ndawalayi…
Read More » -
Anatchezera
Ndazunguzika Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 18 ndipo ndinazunguzika mutu chaka chatha pomwe ndinapezeka ndi kachilombo ka HIVkoma sindinagonepo ndi…
Read More »