Chichewa
-
Anatchezera
Sabata zingapo zapitazi, takhala tikulengeza kuti patsamba lino tizikupatsirani Anatchereza ndi malangizo pamavuto amene mumakumana nawo. Mavutowa akhoza kukhala a…
Read More » -
‘Kudali kosungitsa ndalama’
Ena ukamalowa m’banki amangoganiza kuti chaphindu chochoka mmenemo ndi kusunga kapena kutapa ndalama komatu ena akusimba lokoma chifukwa tikukamba pano…
Read More » -
Kutumiza ana kundende si yankho—Jaji
Jaji wa kubwalo lalikulu (High Court) Justice Annabel Mtalimanja wati kuthamangira kugamula ana achichepere kukagwira ukaidi kundende ndi njira…
Read More » -
Kwaterera kwa ntenje
Mwanunkha m’mudzi mwa Ntenje kwa T/A Machinjiri m’boma la Blantyre komwe osungitsa chitetezo m’midzi (community police) adatibulidwa n’kumangiriridwa pamtengo…
Read More » -
Boma lititeteze, atero achitetezo
Anthu okhwimitsa chitetezo m’mudzi mwa Ntenje, m’dera la T/A Machinjiri m’boma la Blantyre, apempha boma kuti liwateteze ndi kuwasamala…
Read More » -
Chithunzithunzi cha gogo wathu
Mukunyasitsa nkhope mwayambana ndi ndani Munthu wokwiya saoneka bwino Amakhala ngati mtembvo omwe ukanka kumanda Maliro ake ochita kupha ndi…
Read More » -
Manja m’khosi ndi kupsa kwa misika
Pamene nkhani yakupsa kwa misika yayala nthenje m’dziko muno, amalonda ena achita jenkha, kusowa mtengo wogwira katundu wawo atasakazidwa…
Read More » -
Nanawa: Mlowam’malo wa kupitakufa
Matenda a HIV/Edzi asokoneza miyambo ina monga mwambo wa kupitakufa, womwe umapereka mphamvu kwa ‘fisi’ kuti akakonze maliro pocheza…
Read More » -
‘Boma lisavomereze kuchotsa pathupi’
Potsatira zomwe ndinalemba sabata yatha, mmodzi wa awerengi watumiza maganizo ake motere: Rabecca, Ndine mmodzi mwa amene ndimatsatira…
Read More » -
Msewu wa Rumphi-Nyika udzatheka?
Mkonzi, Ndafuna ndipereke chidandaulo kuboma lathu kudzera m’nyuzi yathuyi komanso kwa phungu wa dera lathu la Rumphi West Hon Jacquilline…
Read More » -
Bungwe lilimbikitsa ulimi wa akalulu
Akalulu ndi mtundu wa ziweto zing’onozing’ono zomwe alimi ambiri amanyalanyaza kuweta koma katswiri paulimi wa ziweto zosiyanasiyana, Sute Mwakasungula,…
Read More » -
Ulangizi wabala mwana ku Mulanje
Njala yomwe yakhudza madera ambiri ikuvutanso m’boma la Mulanje komwe anthu akuyembekezereka kutuwa chifukwa cha mvula yanjomba yomwe adalandira…
Read More » -
‘Miyoyo ya Amalawi ili pachiopsezo’
Mkulu wa bungwe loona za umoyo la Malawi Health Equity Network (MHEN) Martha Kwataine wati nzomvetsa chisoni kuti dziko…
Read More » -
Ntchito yasowa, wayamba ulimi wa kabichi
Adabwera m’tauni ya Blantyre kudzasaka ntchito atamaliza Fomu 4. Adaponda paliponse kukasaka ntchito, makalata chilembelenicho ndi satifiketi yake ya…
Read More » -
‘Zulani mitengo ya fodya poopetsa matenda’
Nthawi ino alimi ambiri a fodya ali kalikiriki kufunafuna mbewu, kukonza malo omwe adzalimepo komanso kukonza ndi kufesa nazale.…
Read More » -
Mtima pansi, mayeso A jce alipo chaka chino
Ngati panali kupeneka kulikonse kuti chaka cha 2015/16 kukhala kapena sikukhala mayeso a Junior Certificate of Education (JCE) kutsatira…
Read More » -
Ntchito ilipo
Zilikoliko mawa lino kubwalo la masewero la Kamuzu Stadium kumene mphunzitsi wa timu ya dziko lino Ernest Mtawali akuyembekezeka…
Read More » -
Flames inyamuka mawa
Timu ya Flames ikunyamuka mawa m’dziko muno ulendo ku Tanzania kukaswana ndi timuyi masewero amene alipo Lachitatu pa 7…
Read More » -
Bullets iphana ndi Wanderers lero
Ambiri adakamba kuti mwina masewero a lero pakati pa Bullets ndi Wanderers mu TNM Super League alephereka ponena kuti osewera…
Read More » -
Namrukhunua: Nyumba ya chilhomwe
Kalelo makolo adali ndi njira zawo zochitira zinthu kuti azisangalala ndi kukhala wotetezedwa. Alhomwe nawo ali ndi zimene makolo awo…
Read More »