Chichewa
-
Gule wamkulu akusokoneza
Atsogoleri omwe anali ku msonkhano wa Unesco wokhudza kuteteza masewera a chikhalidwe adaonetsa kuda nkhawa ndi kukula kwa chiwerengero cha…
Read More » -
Mafumu, a m’boma apezeka mu Fisp
Nduna ya za malimidwe, mthirira ndi chitukuko cha madzi Mayi Roza Mbirizi ati athana ndi ogwira ntchito m’boma omwe ayerekeze…
Read More » -
Bilu ya CDF yadutsa popanda wotsutsa
Aphungu a Nyumba ya Malamulo dzana adutsitsa bilu yomwe akufuna kuti apitirize kuyang’anira zitukuko za ndalama za Constituency Development Fund…
Read More » -
Mabwana a apolisi akana kusamuTsidwa
Bwalo lalikulu la milandu ku Lilongwe laletsa boma kusamutsa akuluakulu a apolisi asanu omwe analamulidwa kuti achoke ku polisiko ndi…
Read More » -
Fisp yabwerera m’bwalo
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika Lachisanu adalengeza kuti ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo yabwerera ku Farm…
Read More » -
Otenga mimba atagwiriridwa akhoza kuichotsa—Bwalo
Mtsikana yemwe adagwiriridwa ali ndi zaka 13 n’kupatsidwa mimba ndi bambo wa zaka 60 m’chaka cha 2022, Lachitatu adati adakhutira…
Read More » -
Zaka 4 chifukwa chosiya mwana yekha
Bwalo la milandu ku Nkhotakota lagamula bambo wa zaka 35 a Anthony Phiri kukakhala ku ndende kwa zaka zinayi popezeka…
Read More » -
Njala saweta, atero kadaulo
Kadaulo pa za malimidwe ndi kuonetsetsa kuti anthu ali nchakudya chokwanira a Tamani Nkhono-Mvula aunikira boma kuti lisamalote pa mpando…
Read More » -
Mpikisano pa usipikala, asankha nduna zina
Pomwe aphungu a Nyumba ya Malamulo ayambe kukumana posakhalitsapa, mpikisano ulipo pofuna kusankha masipikala ngakhalenso aphungu amene akhale m’makomiti. Izi…
Read More » -
Kuteteza chilengedwe
Pomwe vuto la mapulasitiki opyapyala likupitirira kuononga chilengedwe, ophunzira awiri a pa sukulu ya ukachenjede ya Mubas adza ndi mapulasitiki…
Read More »