Chichewa
-
‘Boma latipaka mafuta pakamwa’
Ogwira ntchito m’boma ena ati boma lawapaka mafuta pakamwa powalonjeza kuti malipiro awo akwera ndi K61 pa K100 iliyonse kuyambira…
Read More » -
Kusanthula chaka cha ulamuliro wa JB
Pamene dziko lino mawa pa 7 April likhale likusangalala kuti mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda watha chaka akulamulira, ena…
Read More » -
Akhazikitsa ntchito yolimbana ndi Edzi
Boma mogwirizana ndi bungwe la Elizabeth Glaser Pediatric Aids Foundation ati ndondomeko yatsopano yolimbana ndi matenda a Edzi ya ndalama…
Read More » -
Mtsutso pa za makanda odabwitsa
Mtsutso wakula ngati n’koyenera kuti ana obadwa modabwitsa azituluka m’chikuta. Izi zadza mwana wina wankhope yodabwitsa atabadwa kuchipatala cha Salima…
Read More » -
Miyezi inayi idutsa mafumu osalandira mswahala
Nyakwawa komanso magulupu akudandaula kuti matumba awo abooka kaamba koti patha miyezi inayi asakulandira mswahala. T/A Nthache wa ku Mwanza…
Read More » -
Akuti zipolowe zichepe
Zipolowe kaamba ka ndale zomwe zakhala zikuchitika m’dziko muno zikupereka chiopsezo kuchisankho cha chaka chamawa komanso kutekesa mtendere wa dziko…
Read More » -
‘JB watukula amayi, koma ntchito ikadali’
Pamene dziko la Malawi lagwirana manja ndi maiko ena padziko lapansi pokukumbukira tsiku la amayi, Amalawi ena athirapo ndemanga ndi…
Read More » -
Zipolowe atamangidwa Mutharika
Kumangidwa kwa anthu 11 omwe akukhudzidwa ndi nkhani yofuna kulanda boma Bingu wa Mutharika atamwalira sikudakomere anthu ena amene adachita…
Read More » -
Lipoti la imfa ya Bingu latekesa boma, DPP
Pomwe Malawi waona utsi wokhetsa misozi chifukwa cha kumangidwa kwa mamulumuzana a DPP komanso amaudindo ena m’boma, akadaulo pazandale komanso…
Read More » -
Ndalama zakale zitha pa 23 May
Banki yaikulu yakumbutsa mabanki a m’dziko muno kuti ndalama zakale za ‘Chilembwe’ dziko lino zisiya kugwira ntchito pa 22 May.…
Read More »