Chichewa
Mlatho uwu si uli ku Mwanza
Munthu atakutenga ku Blantyre usiku, kukumanga kumaso nkukakusiya pamlatho uwu, ukhoza kuyesa uli ku Mwanza utawerenga chikwangwani ichi. Nkhawa tsopano ikhoza kukhala kuti kubwerera ku Blantyre uyenera kulowera kuti? Komatu mtsinje uwu si uli ku mlatho uwu siuli ku Mwanza koma ku Nsanje! Mtsinjewu umakathira mumtsinje wa Shire. Kumayenda!
Uli ku Chikwawa …..thats where that picture was taken i pass their every day