Chichewa
-
‘Tidangoonana koyamba basi’
Kukumana kudziko la eni n’kudziwana kuti mumachokera kumodzi ndi chinthu chonyaditsa kwambiri moti kwa anthu ena chinansi chimayambira pomwepo…
Read More » -
Kulambira Kalonga Gawa Undi
Tamvapo zambiri za mwambo wa Kulamba. Mongokumbutsana, Kulamba ndi mwambo womwe mafumu Achichewa m’maiko a Malawi, Mozambique ndi Zambia amapezerapo…
Read More » -
Azula chamba, achiyatsa ku KK
Nkhani zoti apolisi alanda kapena azula chamba ndi zina zokhudza mbewu yozunguzayi sizikukata m’boma la Nkhotakota. Lachiwiri sabata ino apolisi…
Read More » -
Bullets yayamba ndi ukali
Timu ya Big Bullets, yomwe ikuteteza chikho cha TNM Super League, yayambanso ndi ukali m’ndime yachiwiri ya ligiyi, kupitiriza zomwe…
Read More » -
FAM ndi Kamuzu Stadium
Sabata yatha kwathu kuno kudabwera alendo a Fifa kudzayendera bwalo la Kamuzu Stadium ngati ndi loyenera kuti mipikisano ya chikho…
Read More » -
Ndege ya ufiti’ ikodwa ku Kasungu
Ngakhale malamulo a dziko lino amakana kumutchula munthu kuti ndi mfiti, Amalawi ambiri amakhulupirira kuti ufitu uliko. Anthu a m’mudzi…
Read More » -
Mlandu wa Savala ukupendekeka
Mlandu wa mayi wa zaka 33, Caroline Savala, yemwe khothi lidamupeza wolakwa pamlandu wakuba ndalama za boma zokwana K84…
Read More » -
Kudali Ku Karonga
Pamene ena amati chikondi sichiona chikhalidwe kapena mtundu wa khungu la munthu, banja la Manaseh Chisiza, mkulu wa bungwe…
Read More » -
Limbani Simenti: Kukangalika pa zoimba
Ku Malawi kuno kuli oimba zauzimu ochuluka. Mmodzi mwa iwo ndi Limbani Simenti yemwe akudziwika bwino. Iyetu amadziwika kwambiri ndi…
Read More » -
ANATCHEZERA
Akundikaikira Anatchereza, Ndine mtsikana wa zaka 17 ndipo ndili Fomu 4. Ndili ndi chibwenzi chomwe ndakhala nacho miyezi 6 ndipo…
Read More » -
Agundidwa akuthawitsa katundu wakuba
Bambo wina wagundidwa ndi galimoto ku Mzuzu pomwe amathawitsa mapaketi awiri a khofi omwe amamuganizira kuti adaba pa Mzuzu…
Read More » -
Mwambo woika maliro a khanda lozizira
Amalawi ngakhale ali ndi miyambo yosiyanasiyana malinga ndi mitundu yawo monga Achewa, Angoni, Atumbuka, Alhomwe, Amang’anga, Asena kaya ndi Ayao,…
Read More » -
Panazale samakololapo!
Flames yalepherana mphamvu ndi Swaziland 2-2 kusonyeza kuti m’gulu L la mpikisano wolimbirana chiko cha Africa Cup of Nations (Afcon)…
Read More » -
A maufulu ayamikira MCP
Akatswiri andale kudzanso mabungwe oimira ufulu wa anthu mdziko muno ayamikila chipani chachikulu chotsutsa boma cha Malawi Congress Party (MCP)…
Read More » -
‘Zilango zophweka zivulaza maalubino’
Miyezi 18 kwa ofuna kugulitsa alubino ku DZ Pali mantha kuti maalubino angapitirire kuona zokhoma m’dziko muno ngati boma silichita…
Read More » -
Dz Young Soccer, ‘Mighty’ adutsa
Chikho cha Standard Bank chayamba ndi moto pamene matimu a asirikali a Kamuzu Barracks ndi Mafco FC aona msana wa…
Read More » -
Chitukuko cha foni
Ndati ndikuuzeni abale anzanga, mbale wina amene anatchona ku Jubeki ndipo anasungidwa ku Lindela kwa nthawi wafika pa Wenela.…
Read More » -
Mavuto osakata pa Wenela
Tidakhala malo aja timakonda pa Wenela ndipo zidaonekeratu kuti zochita zikusowa. Kodi n’kumachitanji pomwe zinthu zikukwera mtengo tsiku ndi…
Read More » -
Evance Masina: Mapanga awiri samuvumbwitsa
Pali mwambi woti ndigwire uku ndi uku pusi anagwa chagada. Penanso amati mapanga awiri avumbwitsa, kutanthauza kuti ndibwino kuchita chinthu…
Read More » -
ANATCHEZERA
Mkazi wanga asabwere? Anatchereza, Ndili ndi zaka 25 ndipo ndili pantchito yokhalira pomwepo. Ndine wokwatira ndipo ndili mwana mmodzi. Abwana…
Read More »