Category: Chichewa

Alendo alanda maudindo mu PP

Kusankhidwa kwa ‘alendo’ ochoka m’zipani zina kukhala m’maudindo onona kuchipani cholamula cha People’s (PP) kungakolezere mavuto kuchipaniko, maka pandawala yolowera kuchisankho cha 2014.
Moto wayaka ku Nkosini

Pasanadutse n’komwe mwezi chilongere Inkosi Yamakosi Gomani Yachisanu ku Ntcheu, fumbi labuka pomwe mbali ina kubanjalo ikukakamiza wogwirizira, Rosemary Malinki kutula pansi udindo komanso…
Kuyezetsa magazi kwayenda bwino

Mlembi wamkulu mu Unduna wa Zaumoyo wati sabata yolimbikitsa kuyezetsa magazi pofuna kudziwa ngati uli ndi kachilombo koyambitsa Edzi idali yapamwamba popeza anthu ochuluka…
Achotsa mavenda popanda ziwawa ku Lilongwe

Kunali njinga yapulula machaka ku Lilongwe Lachisanu lapitalo pomwe anthu mazanamazana amabwerera m’makwawo opanda kanthu m’manja atalephera kukolola posalima akuluakulu awochita malonda munzindawu atatsogolera…
DPP idzudzula boma

Chipani chakale cholamula cha Democratic Progressive (DPP) chati Amalawi angapitirire kusauka ngati boma la chipani cha People’s (PP) silibwera msanga ndi ndondomeko zotukulira anthu…