Nkhani
-
Gulewamkulu, agumula sitolo
Gulewamkulu wina Lachwiri lapitalo akumukayikira kuti adagumula sitolo ina pamsika wa Nkhalambayasamba m’boma la Mchinji ndipo akumukaikira kuti adasakaza katundu…
Read More » -
Ntchito za wedewede zanyanya
Kusowa ndalama zoyendera zitukuko komanso kulekera anthu a kumudzi kugwira ntchito zomangamanga zachitukuko kukuchititsa kuti ntchitozi zizikhala zawedewede, atero akadaulo…
Read More » -
Chigodola chifalikira maboma ena
Matenda a chigodola amene adabuka m’maboma a Blantyre ndi Neno, ayamba kufalikiranso m’maboma ena, watero unduna wa zamalimidwe. Matendawa adayambira…
Read More » -
Apha mwana atasemphena za ndalama
Apolisi m’boma la Mangochi amanga ndi kutsekera m’chitokosi mayi wa zaka 28 chifukwa chomuganizira kuti wapha mwana wake wa zaka…
Read More » -
Afuna kudzikhweza nsanje itakula
Apolisi ya Mponela ku Dowa amanga mayi wa zaka 24 Ketrina Paulo pomuganizira kuti amafuna kudzikhweza ponyansidwa ndi mwamuna wake…
Read More » -
Mangani womenya wotsatira MCP
Chipani chotsutsa cha MCP chapempha apolisi kuti aponye m’chitokosi Isaac Jomo Osman, kadeti wa DPP amene adasautsa ndi kuvulitsa mnyamata…
Read More » -
Chilima saima nawo
Uli dere n’kulinga utayenda naye. Amene akufuna kuti wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Saulos Chilima adzaimire chipanicho pachisankho cha…
Read More » -
Ndikakunyenyani kukovenshoni—APM
Pamene chipani cha DPP chalengeza kuti msonkhano waukulu ulipo mwezi wa mawa, mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika Lachinayi adati…
Read More » -
Chipatala chidzapulumutsa K730m pachaka
Chipatala cha khansa chomwe boma likumanga ku Lilongwe chikatsegulidwa mwezi wa September chaka chino, boma kudzera ku Unduna wa Zaumoyo…
Read More » -
Mswahara wa zifukwa
Munga wadza ndi mafinya omwe. Pamene ena akumwetulira kuti boma lakweza mswahara wa mafumu, mafumu ena ati kukwezaku kuwabweretsera mavuto…
Read More »