Nkhani
-
Chilima akhazikitsa UTM ku Blantyre
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Chilima, mawa akhazikitsa gulu la United Transformation Movement (UTM) ku Njamba mu mzinda…
Read More » -
Wodzaima pa mpando wa pulezidenti azapereka K2m
Bungwe la Malawi Electoral Support Network (Mesn) ladzudzula bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) pokweza ndalama zomwe anthu ofuna kudzaima…
Read More » -
MEC, MCP yakhutira ndi kalembera
Zinthu zasintha. Anthu akulembetsa mwaunyinji m’gawo lachiwiri la kalembera wa zisankho zomwe zidzachitike m’dziko muno chaka cha mawa. Mkulu wa…
Read More » -
La 40 lakwana kwa womata anthu phula
Wakhala akumata anthu phula m’midzi kuti amupatse ndalama ndipo adzakhala ndi mwayi wopeza ngongole kuchokera ku bungwe la Emmanuel International.…
Read More » -
‘Zovota ife ayi’
“Anthu opotsa 3 000 adalembetsa unzika m’dera langa. Lero anthu 1 240 okha ndiwo alembetsa kalembera wa zisankho.” Izi ndizo…
Read More » -
DPP yasankha atsogoleri atsopano
Msonkhano wa masiku atatu wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) womwe umachitikira mu mzinda wa Blantyre wasankha mtsogoleri wa…
Read More » -
Chilima adzapikitsana nawo chaka cha mawa
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, Saulos Chilima, wati adzaima nawo pa zisankho za chaka cha mawa dongosolo lonse loyenera…
Read More » -
Kampeni yayamba ndi ukali
DPP ithamangitsa otsutsa ku Thyolo Kumeneko ndi kunyumba kwa APM—Chakale Kwa eni kulibe mkuwe. Mdima udadza masanasana m’boma la Thyolo…
Read More » -
Kalembera wa zisankho ali mkati
Dzuwa salozerana, kalembera wa zisankho udayamba Lachiwiri m’maboma a Dedza, Salima ndi Kasungu. Izitu zikudza pokonzekera chisankho cha makhansala, aphungu…
Read More » -
Ming’alu m’kalembera wa chisankho cha 2019
Pamene kalembera wa chisankho cha pa 21 May 2019 akuyamba Lachiwiri likudzali, akadaulo ena awona kale ming’alu yakudza chifukwa chokana…
Read More »