Nkhani
-
‘Mgwirizano ungathetse zipolowe’
Mgwirizano pakati pa atsogoleri, ngakhale asemphane maganizo pa ndale ndiko kungathetse zipolowe ndi mikangano ya ndale, atero akadaulo. Iwo adanena…
Read More » -
Anthu 500 000 sadalembetse
Zotsatira za kalembera wachisankho m’gawo loyamba ndi lachiwiri zasonyeza kuti anthu 468 860 omwe amayenera kulembetsa sadalembetse nawo m’kaundulayo. Malingana…
Read More » -
Adzudzula Admarc
Mafumu ndi alimi ena m’zigawo zonse zitatu adandaula kuti msika wa Admarc watsegulidwa mochedwa iwo atagulitsa kale chimanga chawo motchipa…
Read More » -
Kalembera wafika kummwera
Kalembera wa mkaundula wachisankho cha chaka cha mawa wafika m’chigawo cha kummwera tsopano ntchitoyi itakumana ndi zokhoma zosiyanasiyana m’maboma a…
Read More » -
Kuli ziii! za mapulaimale
Pamene ntchito ya kalembera wa chisankho cha pa 21 May 2019 walowa m’gawo lachinayi, zipani zandale zikuluzikulu zikadali duuu, osafuna…
Read More » -
Mamonitala ena sakupezeka kolembetsa
Mamonita a zipani zina sakupezeka m’malo olembetsera mavoti, Tamvani wafukula. Mmalo 7 a m’midzi yomwe Tamvani adazungulira mkati mwa sabatayi,…
Read More » -
‘Mafumu akusunga zitupa za ena’
Pamene gawo lachitatu la kalembera wa chisankho cha pa 21 May 2019 akuyembekezeka kutha mawa m’boma la Lilongwe, anthu ena…
Read More » -
MCP siidakhutire ndi kalembera
Chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chati ngakhale ndime yachiwiri ya kalembera wa zisankho yayenda bwino poyerekeza ndi yoyamba, MEC…
Read More » -
UDF siidaganize za mgwirizano—Atupele
Phungu wa chipani cha United Democratic Front (UDF) wakummwera kwa boma la Balaka, Lucius Banda, wapempha chipanicho kuti chilowe mu…
Read More » -
UTM Ilembetsa ngatichipani—Malunga
Ulendo wapsa. Ali ndi mwana agwiritse. Eni basiyo akuti siiphwa matayala mpaka ikafika ku zisankho zapatatu za chaka cha mawa.…
Read More »