Nkhani
-
‘Lingalirani bwino musanathane ndi fodya’
Akatswiri komanso alimi ati dziko la Malawi likuyenera kulingalira mozama lisadagonjere khumbo la bungwe la zaumoyo padziko lonse la World…
Read More » -
Palibe mlendo ku MCP—Munthali
Pomwe chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chidachititsa msonkhano wake waukulu kumathero a sabata yapitayi mwa mpanimpani pothawa ziletso ku…
Read More » -
‘Chilonda chatukusira mu DPP’
Bwerani poyera mulankhule kwa Amalawi. Awa ndi mawu a akadaulo pa ndale pamene alangiza mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika…
Read More » -
New grain technology excites govt
The Ministry of Agriculture, Irrigation and Water Development has challenged innovators to come up with more technologies aimed at cutting…
Read More » -
Wopanda chiphaso cha nzika sadzavota—MEC
Bungwe loyendetsa zisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) latsimikiza kuti chiphaso chakale chovotera sichidzanunkha kanthu pachisankho cha 2019. Wapampando wa…
Read More » -
Moto buuu! 2019 yafukiza zipani
Fumbi lachita kobooo! m’zipani pamene kwangotsala chaka chimodzi kuti chisankho cha patatu chichitike m’dziko muno. Chisankho cha patatu chidzakhalako pa…
Read More » -
Akufuna boma likweze malipiro
Bungwe loona za ufulu wa anthu ogwira ntchito la Malawi Congress of Trade Union (MCTU) lapempha boma kuti likweze mlingo…
Read More » -
Apayoniya akana zionetsero
Amene adali a Malawi Young Pioneers (MYP) omwe atha miyezi 10 akubindikira ku Lilongwe kufuna ndalama zawo zopumira pantchito ndipo…
Read More » -
Amalawi alankhula: Masiku 30, boma liyankhe—Gift Trapence
Malawi adayaka moto dzulo m’zigawo zonse pamene anthu adayenda pokhumudwa ndi ntchito za boma la DPP. Mfundo yamangidwa ndiyoti boma…
Read More » -
‘Mundibwezere voti yanga’, amalawi athafulira APM pazionetsero
Amalawi athera Chichewa mtsogoleri wa dziko lino komanso nduna zake pa zionetsero zomwe zidachitika Lachisau. Zionetserozo zidatsogoleredwa ndi amipingo, amabungwe…
Read More »