Nkhani
-
Wopha Wame akasewenza moyo wake wonse
Bwalo la milandu lalikulu m’boma la Salima Lachitatu lidagamula Limbani Maliro, mnyamata yemwe adapha Mlaliki Shadreck Wame kukasewenza moyo wake…
Read More » -
‘Kusintha lamulo la ufiti kwachedwa udyo’
Kuchedwa kwa ntchito yosintha lamulo lokhudza zaufiti kukuchititsa kuti okalamba amene akuwaganizira kuti ndi mfiti apitirire kuzunzidwa komanso kuphedwa, atero…
Read More » -
Adindo akhudzidwa pa imfa ya Masambuka
Kusowa kwa mnyamata wa chialubino m’boma la Machinga kwavumbulutsa zinthu zoziritsa thupi. Macdonald Masambuka wa zaka 22 yemwe ankachokera…
Read More » -
Samalani ndi sikelo za chinyengo—MBS
Nthawi yokolola yakwana, pomwe alimi amataya zokolola zawo kwa mavenda akuba amene amamanga sikelo pofuna kuliza alimi. Koma bungwe loona…
Read More » -
Ambwandira msilikali ku Salima
Apolisi a chigawo chapakati abatha msilikali wa nkhondo ndi anthu ena awiri powaganizira kuti adapezeka ndi chamba popanda chilolezo. Msilikaliyu,…
Read More » -
Chipatala cha khansa chitheka September
Odwala khansa ayembekezere kupuma umoyo wina. Chipatala chachikulu chothana ndi matendawa chitsegulidwa September chaka chino mumzinda wa Lilongwe. Nduna ya…
Read More » -
Akupopa zimbudzi pochepetsa matenda
Ena zimbudzi zawo zikadzadza amagwetsa ndi kukumba china. Uku ndi kutha malo. Lero zinasintha chifukwa khonsolo ya Blantyre mogwirizana ndi…
Read More » -
Kuli ziii! Pa za mthandizi
Kwangoti zii! Nkhawa yagunda ngati ntchito za mthandizi zomwe anthu amalandira kangachepe akalima msewu ichitike popeza nthawi yake yadutsa osamvapo…
Read More » -
Milandu yachepa ku Blantyre
Milandu yosiyanasiyana mu mzindawa Blantyre yatsika kuchoka pa 328 mu February chaka chatha kufika pa 204 mwezi omwewo chaka…
Read More » -
Maphunziro alowa libolonje
Mphunzitsimmodzi, ana 110 Komaaphunzitsi 10 000 akusowantchito Dziko la Malawi lalephera kukwaniritsa loto lake loti pofika chaka chino, mphunzitsi mmodzi…
Read More »