Nkhani
-
Adzudzula JB zomanga mfumu
Mphunzitsi wa za malamulo kusukulu yaukachenjede ya Chancellor College Mwiza Nkhata wati ndi zodabwitsa kuti mtsogoleri wa dziko lino Joyce…
Read More » -
Mafumu aluzanitse mtundu
Nthawi ya mwambo wa Achewa wa Kulamba yafikanso. Paja chikhalidwe ndiye mizu ya mtundu ulionse. Achewa amasonkhana malo amodzi monga…
Read More » -
Amayi chepetsani zotsirana phalazi
Kawirikawiri nkhani ya nkhanza za m’mbanja imagonera abambo kuti ndiwo ali patsogolo kuzunza amayi. Tikaonetsetsa chiwerengero cha nkhanza za m’banja…
Read More » -
Za pasipoti ya Gaba sizikumveka
Sabatayi yakhala yomvetsa mutu ndi nkhani ya Gabadihno Mhango. Zachitika m’sabatayi aganyu zatiwawa ndipo tikufuna bungwe la FAM komanso timu…
Read More » -
Jombo ikudiliza matimu
Chalaka bakha nkhuku singatole. Linda madzi apite ndiye udziti wadala. Miyambiyi ndiyo idatsanuka m’sabatayi kaamba ka jombo yomwe idathudzula Nyerere…
Read More » -
Amalawi apindulanji ndi kutsogolera Sadc
Akuluakulu pa zachuma komanso mafumu m’dziko muno ati mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda afunika masomphenya kuti dziko lino lipindule…
Read More » -
Amalawi apindulanji?
Sabata yatha mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda adakhala wapampando wa bungwe la mgwirizano wa maiko a kumwera kwa Africa…
Read More » -
Kusiya ana akunjira muwilo
Sabata yathayi mmodzi wa awerengi a tsambali adafunsapo pankhani ya ana akunjira, makamaka mounikirapo pa zikalata zomwe makolo owabereka amasiya…
Read More » -
Chikho cha Carlsberg chafika pachimake
Thambo lagwa, chikho cha Carlsberg chaka chino chabwera ndi zake pamene anyamata ovala jombo atenga malo kugwedula matimu omwe amakula…
Read More » -
Chakwera angadze ndi kalumo kakuthwa
Mlendo ndiye adza ndi kalumo kakuthwa. Akadaulo pandale ati kusankhidwa kwa mbusa Dr Lazarus Chakwera kukhala mtsogoleri wa chipani chachikulu…
Read More »