Nkhani

  • Adandaula za misewu yosakonzedwa

    Pomwe anthu akhala akuitsotsombetsa nthambi ya Road Fund Administration ati ponena kuti ikukanika kukonza misewu ya m’dziko muno chonsecho nthambiyo…

    Read More »
  • Kungoimvera fungo Khrisimasi

    Kwangotsala masiku anayi kuti tsiku limene Akhristu amakumbukira kubadwa kwa Yesu Khristu. Kafungo ka mpunga, nyama yootcha, nkhuku yowiritsa ngakhale…

    Read More »
  • Gule wamkulu akusokoneza

    Atsogoleri omwe anali ku msonkhano wa Unesco wokhudza kuteteza masewera a chikhalidwe adaonetsa kuda nkhawa ndi kukula kwa chiwerengero cha…

    Read More »
  • Mafumu, a m’boma apezeka mu Fisp

    Nduna ya za malimidwe, mthirira ndi chitukuko cha madzi Mayi Roza Mbirizi ati athana ndi ogwira ntchito m’boma omwe ayerekeze…

    Read More »
  • Bilu ya CDF yadutsa popanda wotsutsa

    Aphungu a Nyumba ya Malamulo dzana adutsitsa bilu yomwe akufuna kuti apitirize kuyang’anira zitukuko za ndalama za Constituency Development Fund…

    Read More »
  • Mabwana a apolisi akana kusamuTsidwa

    Bwalo lalikulu la milandu ku Lilongwe laletsa boma kusamutsa akuluakulu a apolisi asanu omwe analamulidwa kuti achoke ku polisiko ndi…

    Read More »
  • Fisp yabwerera m’bwalo

    Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika Lachisanu adalengeza kuti ndondomeko ya zipangizo za ulimi zotsika mtengo yabwerera ku Farm…

    Read More »
  • Otenga mimba atagwiriridwa akhoza kuichotsa—Bwalo

    Mtsikana yemwe adagwiriridwa ali ndi zaka 13 n’kupatsidwa mimba ndi bambo wa zaka 60 m’chaka cha 2022, Lachitatu adati adakhutira…

    Read More »
  • Zaka 4 chifukwa chosiya mwana yekha

    Bwalo la milandu ku Nkhotakota lagamula bambo wa zaka 35 a Anthony Phiri kukakhala ku ndende kwa zaka zinayi popezeka…

    Read More »
  • Njala saweta, atero kadaulo

    Kadaulo pa za malimidwe ndi kuonetsetsa kuti anthu ali nchakudya chokwanira a Tamani Nkhono-Mvula aunikira boma kuti lisamalote pa mpando…

    Read More »
Back to top button