Nkhani
-
Dolo ndi ndani mu chipeta ichi?
Pamene kwatsala masiku atatu okha kuti nzika za dziko lino zivote, atsogoleri omwe akuimira pa mipando ya upulezidenti, uphungu wa…
Read More » -
Kandideti walonjeza nsapato, maendedwe otsika mtengo
Malonjezo pa nthawi ya chisankho si achilendo. Koma pali ena oti ukamva, umagwedeza mutu. Yemwe adzaimire chipani cha UTM ku…
Read More » -
Kandideti wa MCP wapambana anthu asanavote
Bungwe la zachisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lati yemwe amaimira chipani cha Malawi Congress Party (MCP) ku dera la…
Read More » -
Aphungu asintha lamulo
Fumbi lakhazikika lokhudza komwe anthu omwe adzakhale akugwira ntchito za chisankho pa nthawi yovota pa September 16 adzaponyere voti yawo.…
Read More » -
MEC yasefa ma kandideti, 17 adutsa
Pomwe kampeni ili mkati, bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) latulutsa maina a ma kandideti omwe akwaniritsa zofunika pa mpando…
Read More » -
CDF idatsamwitsa aphungu, makhansala
Pomwe aphungu ndi makhansala amene agwira ntchito yawo kwa zaka 6 akwangula ntchito yawo Lachitatu, akadaulo ndi nzika zina anenetsa…
Read More » -
Miyezi 30 kwa ogona ndi ng’ombe
Bwalo la Chitipa Senior Resident Magistrate, Lolemba pa 14 July 2025, lidagamula bambo wina wa zaka 24 a James Mtambo,…
Read More » -
Adandaula za nyumba ya chisoni
Anthu okhala m’dera la Lisungwi m’boma la Neno adandaula ndi kusagwira ntchito kwa nyumba ya chisoni. Nyumba ya chisoni ya…
Read More » -
Amanga womuganizira kuba chimanga
Bwalo la First Grade Magistrate ku Thyolo masiku apitawa lidagamula bambo Mphatso Mateyu, omwe amachokera m’mudzi mwa Changata, m’dera la…
Read More » -
Kampeni iyamba lolemba
Chisankho cha 2025 chifika gawo lina Lolemba likudzali pomwe bungwe loyendetsa zisankho la MEC lidzakhazikitse misonkhano yokopa anthu. Malingana ndi…
Read More »