Nkhani
-
Lorani mtendere ulamulire
Kampeni ikutha mawa. Atsogoleri atambasula mfundo zawo za chitukuko zomwe zili m’manifesto. Nawo mabungwe a Oxfam ndi Women Legal Resource…
Read More » -
Mabungwe akufuna malamulo okhudza AI
Mabungwe a Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR) ndi Malawi Human Rights Commission (MHRC) apempha boma kuti liunikenso malamulo…
Read More » -
Zikhalidwe zikukhomerera amayi
Wapampando wa Engalaweni Women Group a Mervis Mvula akuti zikhalidwe, zikhulupiriro ndi umphawi ndizo zikulepheretsa amayi ambiri kulowa ndale. A…
Read More » -
Dolo ndi ndani mu chipeta ichi?
Pamene kwatsala masiku atatu okha kuti nzika za dziko lino zivote, atsogoleri omwe akuimira pa mipando ya upulezidenti, uphungu wa…
Read More » -
Kandideti walonjeza nsapato, maendedwe otsika mtengo
Malonjezo pa nthawi ya chisankho si achilendo. Koma pali ena oti ukamva, umagwedeza mutu. Yemwe adzaimire chipani cha UTM ku…
Read More » -
Kandideti wa MCP wapambana anthu asanavote
Bungwe la zachisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) lati yemwe amaimira chipani cha Malawi Congress Party (MCP) ku dera la…
Read More » -
Aphungu asintha lamulo
Fumbi lakhazikika lokhudza komwe anthu omwe adzakhale akugwira ntchito za chisankho pa nthawi yovota pa September 16 adzaponyere voti yawo.…
Read More » -
MEC yasefa ma kandideti, 17 adutsa
Pomwe kampeni ili mkati, bungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) latulutsa maina a ma kandideti omwe akwaniritsa zofunika pa mpando…
Read More » -
CDF idatsamwitsa aphungu, makhansala
Pomwe aphungu ndi makhansala amene agwira ntchito yawo kwa zaka 6 akwangula ntchito yawo Lachitatu, akadaulo ndi nzika zina anenetsa…
Read More » -
Miyezi 30 kwa ogona ndi ng’ombe
Bwalo la Chitipa Senior Resident Magistrate, Lolemba pa 14 July 2025, lidagamula bambo wina wa zaka 24 a James Mtambo,…
Read More »