Nkhani
-
‘Wogona’ ndi mwana wake pofuna mfumba agwidwa
Ndani adanena kuti chizimba cha mfumba ndi kugona ndi mwana wako? Izi zachitika ku Dedza komwe apolisi anjata bambo wa…
Read More » -
Amayi abisa katundu wa K16 000 mu panti
Ukathyali wakasololedwe wachitika pamalo omwetsera mafuta a Puma pa Wenela pomwe apolisi adanjata mkulu wina wa ku Zambia pomuganizira kuti…
Read More » -
Mpingo ukana mbusa womangidwa za zitupa
Mpingo wa Lord’s Chosen Charismatic Revival Ministries (LCCRM) wakana zomwe munthu wina wa ku Cameroon adauza nthambi yoona za anthu…
Read More » -
Maneb ikhutila ndi mayeso a sitandade 8
Bungwe loyendetsa mayeso la Malawi National Examinations Board (Maneb) lati lakhutira ndi mmene mayeso a Sitandade 8 ayambira. Mkulu wa…
Read More » -
Anthu a ku Likoma alirira Ilala
Anthu okhala pazilumba za Likoma ndi Chizumulu ati akulira ndipo moyo ukutentha chifukwa cha kusiya kuyenda kwa sitima ya Ilala.…
Read More » -
Bajeti iganizire mavuto a anthu
Ndondomeko ya chuma ndiyo chiyembekezo chachikulu tsopano chomwe chingachepetse mavuto omwe anthu akukumana nawo kaamba ka kukwera mitengo ya zinthu…
Read More » -
Apolisi anjatidwa pokhudzidwa ndi ophedwa pa zionetsero
Apolisi asanu ndi anayi adatengedwa m’sabatayi powaganizira kuti akudziwapo kanthu pa za ena amene adaphedwa pazionetsero za pa 20 Julaye…
Read More » -
‘Boma likweza malipiro’
Ogwira ntchito angasimbe lokoma ngati ganizo la unduna wa zantchito lokweza malipiro otsikitsitsa amene amalandira lingafitsidwe. Izi zadza ogwira ntchito…
Read More » -
Zipolowe zikuphulika
Pamene tikuyandikira chaka cha 2014 pomwe Amalawi akuyembekeza chisankho cha magawo atatu chosankha Pulezidenti, aphungu a Kunyumba ya Malamulo ndi…
Read More » -
Konvenshoni ya MCP yalephereka
Chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chati msonkhano wake waukulu wa konvenshoni umene umayenera kukhalapo pakati pa lero ndi Lolemba…
Read More »