Nkhani
-
Mandela adwala mwa kayakakaya ku South Africa
Mtsogoleri wakale wa dziko la South Africa Nelson Mandela adali kudwalika zedi pachipatala china ku Pretoria m’dzikomo. Pomwe timasindikiza Tamvani…
Read More » -
‘Lamulo la chuma cha pulezidenti liunikidwenso’
Mmodzi mwa akatswiri a za malamulo Edge Kanyongolo wati lamulo lomwe likukamba za katundu ndi chuma cha atsogoleri a dziko…
Read More » -
Mayi athokoza ataomboledwa
Maness Thom wa Zaka 65 wathokoza bungwe losakhulupirira kuti kunjaku kuli Mulungu komanso mphamvu za mizimu ina la Association of…
Read More » -
Wa zaka 70 wofuna kugwiririra amangidwa
Bwalo lamilandu la Dedza Lachiwiri lagamula gogo wa zaka 70 kuti akaseweze kundende zaka zinayi kaamba kofuna kugwiririra mdzukulu wake…
Read More » -
Nanga wapolisi ataphofomoka?
Masiku ano sichikhala chachilendo kuona apolisi atakwera galimoto mosayenera. Ngakhale ntchito yawo n’kuonetsetsa kuti malamulo akutsatidwa, ngakhale pamsewu, apolisiwo ndiwo…
Read More » -
Apolisi aphunzira kagwiridwe ka ntchito yawo
Polisi ya Nkhotakota yakhala yoyamba kuphunzitsidwa za momwe angagwirire ntchito yawo panthawi ya zipolowe komanso zionetsero. Maphunzirowa akudza poyang’anira chisankho…
Read More » -
‘BAMBO ATHOTHA MWANA’
Bambo wina m’mudzi mwa Nchada kwa T/A Nthondo ku Ntchisi amulamula kuti alipe mkazi wake ndi mwana wake wamkazi wa…
Read More » -
Kudziongola ngati zenizeni, koma ayi
Lachitatu sabata yatha anyamata a Flames, ngakhale adapeza mwayi wochuluka kuposa Namibia, adalepherana ndi timuyo mumpikisano wolimbirana malo ku mpikisano…
Read More » -
Woba chiponde ku Chiladzulu agwidwa
Bwalo la Chiradzulu layamba kuzenga mlandu Operations Manager wa kampane yolondera ya Global Communications Centre pomuganizira mlandu woba chiponde cha…
Read More » -
Mkulu wa kunyumba ya chisoni agwidwa ndi ziwalo
Abambo awiri omwe amagwira ntchito kunyumba yachisoni kuchipatala cha Kamuzu Central (KCH) akuzengedwa mlandu wodula maliseche a mtembo wa munthu…
Read More »