Nkhani
-
‘Ndale zachibwana zalowa ku MCP’
Kadaulo wa ndale kusukulu ya ukachenjede ya Chancellor College Blessings Chinsinga wati chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chalowa chibwana,…
Read More » -
Ulemu ulibe mkazi kaya mwamuna
Ulemu ndi khalidwe lofunika pamoyo wa munthu wina aliyense—wamwamuna kapena wamkazi—choncho mtsogoleri wadziko lino sadaphonye kwenikweni masiku apitawa pomwe adakumbutsa…
Read More » -
Joyce Banda akumana ndi mafumu, otsutsa azizwa
Mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda Lachinayi adakumana ndi mafumu a m’dziko muno, zomwe zidachititsa otsutsa boma ena kuzizwa. Banda…
Read More » -
Kaundula wa mavoti akuyenda bwino
A Malawi m’madera ena adakhamukira kumalo olembetsa maina awo m’kaundula wa chisankho cha pa 20 May 2014. Malinga ndi mphunzitsi…
Read More » -
‘Chihana abweretse umboni za chuma cha Bingu’
Chipani cha DPP chati Yeremiah Chihana, amene adavumbulutsa zoti mtsogoleri wakale wa dziko lino Bingu wa Mutharika adali ndi chuma…
Read More » -
Chisankho chanunkhira, koma ku MCP kuli chuuu!
Pamene anthu m’madera ena ayambe kulembetsa maina awo m’kalembera wa chisankho cha magawo atatu cha chaka chamawa Lolemba likudzali, sizidadziwikebe…
Read More » -
Malawi wapindulanji muzaka 49?
Pamene dziko lino lero likukumbukira kuti lakwanitsa zaka 49 lili pa ufulu wodzilamulira, Amalawi ena ati ngakhale pali zina zolozeka…
Read More » -
Aphunzitsi adzawalabadire ndani?
Ambiri timadzudzula kujombajomba komanso kusalimbikira ntchito kwa aphunzitsi m’sukulu za boma. Mchitidwewu ngopititsa pansi maphunziro chifukwa ophunzira amachoka kusukulu asanasulidwe…
Read More » -
Scova adatani?
Nkhani yavuta m’sabatayi ndi ya Nyerere kuti zidagenda pomwe zimasewera ndi Blue Eagles. Aganyu sitivomereza kugenda ndipo tafuna timvetsetse chomwe…
Read More » -
Ntchito yomanga njanji iima
Ntchito yomanga njanji yochoka ku Kachaso kupita ku Nkaya ayiimitsa mpaka kampani ya Mota-Engel ndi ogwira ntchito kukampaniyo atamvana chimodzi.…
Read More »