Nkhani
-
Wailesi ya Dzimwe ikusowa thandizo ku Mangochi
Nyumba youlutsira mawu ya Dzimwe Community Radio ku MonkeyBay m’boma la Mangochi yapempha thandizo lomangira ofesi komanso kugula zida zoulutsira…
Read More » -
Konvenshoni ya MCP pa 28 April
Pamene chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chatsimikiza kuti msonkhano wake waukulu wokasankha atsogoleri udzachitika pa 28 ndi 29 Epulo,…
Read More » -
Olephera asatuluke DPP—Mutharika
EMMANUEL MUWAMBAYemwe anali mtsogoleri wogwirizira mpando wa pulezidenti wa chipani cha DPP, Peter Mutharika, Lachinayi adalangiza omwe amapikisana nawo pofuna…
Read More » -
Tikolola chimanga chochuluka—Nduna
Nduna ya zamalimidwe komanso kuonetsetsa kuti m’dziko muno muli chakudya chokwanira, Peter Mwanza yati undunawu ukulosera kuti chaka chino dziko…
Read More » -
Amayi omwe ali ndi kachilombo akufuna mudzi wawo
Amayi omwe ali ndi kachilombo koyambitsa matenda a Edzi ka HIV kwa T/A Kalolo ku Lilongwe apempha boma kuti liwapatse…
Read More » -
‘Boma latipaka mafuta pakamwa’
Ogwira ntchito m’boma ena ati boma lawapaka mafuta pakamwa powalonjeza kuti malipiro awo akwera ndi K61 pa K100 iliyonse kuyambira…
Read More » -
Kusanthula chaka cha ulamuliro wa JB
Pamene dziko lino mawa pa 7 April likhale likusangalala kuti mtsogoleri wa dziko lino Joyce Banda watha chaka akulamulira, ena…
Read More » -
Akhazikitsa ntchito yolimbana ndi Edzi
Boma mogwirizana ndi bungwe la Elizabeth Glaser Pediatric Aids Foundation ati ndondomeko yatsopano yolimbana ndi matenda a Edzi ya ndalama…
Read More » -
Mtsutso pa za makanda odabwitsa
Mtsutso wakula ngati n’koyenera kuti ana obadwa modabwitsa azituluka m’chikuta. Izi zadza mwana wina wankhope yodabwitsa atabadwa kuchipatala cha Salima…
Read More » -
Miyezi inayi idutsa mafumu osalandira mswahala
Nyakwawa komanso magulupu akudandaula kuti matumba awo abooka kaamba koti patha miyezi inayi asakulandira mswahala. T/A Nthache wa ku Mwanza…
Read More »