Chichewa
-
Mbuzi ndi zosavuta Kusamalira, kudyetsa
Mlangizi wa ziweto wa ku G&LM Vet Services, Edwin Nyondo, wapempha alimi ambuzi kuti aziika mtima pa ulimiwu kuti azipeza…
Read More » -
Amapita kukagula zomwera tiyi
Kukumana kwanga ndi mkazi wanga kudali koseketsa kwambiri chifukwa ndidakuna naye akupita kukagula shuga ku golosale komanso zomwera tiyi,” adalongosola…
Read More » -
Chaka chomwe zogwiririra Ana ndi amayi zanyanya
November 21 2020. Kulira kwa khanda la miyezi 5 kudamveka m’boma la Zomba. Khandali silimalira chifukwa cha njala kapena kuti…
Read More » -
HRDC yawonanji m’boma la Tonse
Anthu ambiri akhala akudabwa kuti gulu lomwe lakhala likutsogolera Amalawi pa ziwonetsero zokhudza kusagwirizana ndi momwe boma likuyendera la Human…
Read More » -
Mphini yobwereza Idawala mu 2020
Chaka cha 2020 chidali chaka cha pelete chomwe podzuka m’mawa wa tsiku la pa June 27 2020, Amalawi adadzidzimuka kuona…
Read More » -
Thirani feteleza nthawi Yabwino, moyenera
Mlimi akhoza kukonza m’munda moyenera, kubzala mbewu yabwino ndi moyambirira komanso kuthana ndi tchire koma osapeza zokolola zoyenera akaphonya pankhani…
Read More » -
Zisangalalo zafika, samalani
Yafika nyengo ya zisangalalo za Khrisimasi ndi Nyuwere ndipo ena ayamba kale mapwando pomwe ena akukonzekera masangalalidwe osiyanasiyana monga kupita…
Read More » -
Mademo ayambika
Gulu lomwe lakhala likudzudzula boma la Tonse Alliance chilowereni m’bomamo la Centre for Democracy and Economic Development Initiative (Cdedi) mogwirizana…
Read More » -
Makhansala aderera alawansi
Kucha kwa Lolemba lapitali Amalawi adadzuka ndi nkhani yododometsa kuona adindo (makhansala) akulalata poyera kudelera alawansi ya K20 000 ndipo…
Read More » -
Athotha a kabaza opanda mapepala
Boma lalamula apolisi m’dziko muno kuti athothe akabaza onse a njinga zamoto zopanda mapepala oziyenereza kuyenda pamsewu ndi kumanyamula anthu.…
Read More »