Chichewa
-
Aphungu akumana lolemba
Aphungu a Nyumba ya Malamulo ayamba kuunika momwe bajeti ya 2020 mpaka chaka chino yayendera m’miyezi 6 yoyamba Lolemba likudzali…
Read More » -
Ndi ana omwe akudzipha
Bambo wina adadzipha m’boma la Chiradzulu atazindikira kuti mkazi wake amachita ubwenzi wa mseri ndi mchimwene wake. Izitu zidaululika pomwe…
Read More » -
Mfutso mpatali
Chilimwe chikuyandikira ndipo chakudya cha ziweto chili paliponse. Mkulu wa zaulimi wa ziweto m’boma la Kasungu akuti apa ndi pamene…
Read More » -
Mtsutso pa zotsegulira sukulu lolemba
Pulani ya boma yoti sukulu zikuyenera kutsegulidwanso Lolemba likudzali yasinthidwanso ndipo tsopano Unduna wa zamaphunziro ukufuna kuti uwunikenso m’mene mliri…
Read More » -
Akhumudwa ndi kusowa kwa mnyamata wachialubino
Magulu omenyera ufulu wa anthu komanso bungwe la anthu achialubino la Association for People with Albinism in Malawi (Apam) ati…
Read More » -
Anatchezera
Za Chikondi ndi chibwenziAgogo,Kodi chibwenzi ndi chikondi ndi zosiyana bwanji? Mwina funso limeneli likhoza kuoneka ngati lopanda nzeru koma kwa…
Read More » -
‘Yunifolomu ya polisi idamukhala’
Padali pa 14 June 2017 pomwe Richard Chitsamba adamuona koyamba mkazi wake Fosina Vasulu. Apa nkuti awiriwo akuweruka m’zintchito mwawo…
Read More » -
Amapita kukagula zomwera tiyi
Kukumana kwanga ndi mkazi wanga kudali koseketsa kwambiri chifukwa ndidakuna naye akupita kukagula shuga ku golosale komanso zomwera tiyi,” adalongosola…
Read More » -
Anatchezera
Takulandiraninso mu 2021 Ndikufuna ndikulandireni m’chaka cha 2021. Chaka chatha lidali thumba la zambiri. M’chakachi zina zidali zokoma, koma zina…
Read More » -
Odzipha akuchuluka
M’chaka cha 2020 chiwerengero cha anthu odzipha chidakwera poyerekeza ndi cha m’chaka cha 2019. Kafukufuku wa apolisi akuonetsa ku chiwerengerochi…
Read More »