Chichewa
-
Katemera wa covid ayamba
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera Lachinayi adalandira katemera wa matenda a Covid 19 pachipatala chapadera cha matendawa chomwe achikhazikitsa…
Read More » -
Phindu la kusankhiratu fodya pothyola
Mlimi akasankhiratu fodya wake pamene akuthyola, kusoka ndi kuumitsa, amapeza phindu lochuluka kusiyana ndi kumangomusakaniza ndi kudzasankha atamuumitsa kale. Alangizi…
Read More » -
Akana ndalama za Covid-19
Anthu ayera m’manja. Ndalama za Covid zatuluka. Komatu mayi wina mumzinda wa Mzuzu wakana kulandira ndalamazi akuti nzasataniki. Mayiyo akuti…
Read More » -
Mipingo yakonzeka zophunzitsa anthu za katemera wa Covid 19
Thunthu loyamba la katemera wa Covid 19 lidafika mziko muno sabata ikuthayi ndipo malingana ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus…
Read More » -
Boma ligulitsa chimanga pamtengo wa sabuside
Kadaulo pazamalimidwe Tamani Nkhono-Mvula wati boma likhale ndi ndondomeko yokhwima yogulitsira chimanga pa mtengo wa sabuside ngati momwe lakonzera poopa…
Read More » -
Mtsutso pa zoika a Covid-19
Kusamvana kukupitirira pakati pa achipatala ndi anthu pa ndondomekoyoyenera kutsatidwa munthu yemwe amadwala matenda a Covid-19 akamwalira. Pomwe achipatala akuti…
Read More » -
Amwalira atathawa m’chipatala
Mayi wina wa zaka zapafupifupi 60 adamwalira maola anayi,atathawitsidwa m’chipatala cha paboma la Nkhotakota ndi abale ake, atamupeza ndi matenda…
Read More » -
‘Osakondera odya nawo K6.2 biliyoni’
Bota layamba kuwira mumphika wa K6.2 biliyoni yothandiza polimbana ndi matenda a Covid 19 yomwe ikumveka kuti idatafunidwa ndipo akuluakulu…
Read More » -
Sukulu zitsegulidwanso
Mkokemkoke umene udalipo pakati pa aphunzitsi ndi boma watha tsopano ndipo ophunzira amayenera kubwerera kusukulu dzulo Lachisanu. Izi zadza kutsatira…
Read More » -
Ayamikira boma pa ganizo lotsegulanso sukulu
Komiti yotsogolera kulimbana ndi matenda a Covid yalengeza kuti sukulu zonse zitsegulidwe Lolemba likudzali pa 22 February. Nduna ya zaumoyo…
Read More »