Chichewa
-
Anthu 49 afa ndi mphenzi
Mphezi zavuta chaka chino. Pofika lero anthu 49 aphedwa ndi mphenzi chiyambireni nyengo ya mvula, poyerekeza ndi 32 omwe adafa…
Read More » -
Luso la Joe Kellz mpatali
Kellz ndi katakwe ku nkhani ya maimbidwe. Mwachidule, tingoti Kellz amatha. Masiku apitawa iye adatulutsa nyimbo yokumbukira luso la katswiri…
Read More » -
Tambala walira
Chipani cha Malawi Congress Party (MCP) chapeza mipando 4 mwa mipando 7 ya aphungu yomwe zipani komanso oima paokha amalimbirana…
Read More » -
Aphunzitsi akhoza kuyambanso sitalaka
Masiku 7 omwe bungwe la aphunzitsi la Teachers Union of Malawi (TUM) lidapereka ku boma kuti liwapatse ndalama zomwe adapangana…
Read More » -
Mukufuna kulima chamba?
Kwa nthawi yaitali, chamba chakhala chikulimidwa m’dziko muno mozembera malamulo. Komatu makono kwadza chamba chosazunguza bongo chimene akuchitama kuti chikhonza…
Read More » -
Anthu ochuluka akufuna katemera
Pomwe zipatala zambiri zayamba kubaya katemera woteteza ku matenda a Corona mu gawo loyamba, achipatala ati anthu ankhaninkhani omwe sali…
Read More » -
Zokolola zichuluka
Unduna wa zamalimidwe wati chaka chino dziko la Malawi likolola chimanga chokwana matani 4.4 miliyoni chomwe nchopitilira mlingo omwe dziko…
Read More » -
Tikwanitsa lonjezo lililonse—Chakwera
Mtsogoleri wadziko lino Lazarus Chakwera wati Amalawi asamvere za anthu omwe akufalitsa kuti boma lake lafotsera malonjezo omwe lidapereka pa…
Read More » -
Kutakata ndi ulimi wa mitengo ya zipatso
Pamene alimi ena akukangalika ndi ulimi wa ziweto kapena mbewu zina, Pilirani Tendai Khoza adapeza mtaji pa ulimi wa mitengo…
Read More » -
Zigamulo zogwirira zikufooketsa
Sabata yatha inali imodzi mwa sabata yomwe inaika pa mbalambanda kuya kwa nkhani zogwiririra m’dziko muno. Pomwe bambo wina wa…
Read More »