‘Masiku 100 a Mutharika sanakome’

Mtsogoleriwa dziko lino Peter Mutharika sabata yatha adakwanitsa masiku 100 pampando wa pulezidenti koma panyengoyi sadamwe wa mkaka..

ChiulutsirenikupambanakwaMutharika, Amalawi ataponya voti pa 21 May 2019, dziko la Malawi layendam’mikwingwirimayokhayokhapomweAmalawienaakhalaakuchitazionetserozosonyezakusakondwandimomwechisankhochichidayendera.

Mutharika kulandira lupanga la ulemu atapambana chisankho

Ngakhalemalamulo a dziko lino amaperekampatawochitazionetserozamtendere, zionetserozaulendounozaonetsaAmalawizambiripomwekatundu, bizinesi, galimotozaanthukomansozabomazawonongedwa. Izizafikapovutakwambirimpakabwalolailandusabatayathalidagamulakutipasachitikensozionetserokwamasiku 14 kutimbalizotsutsanazikambiranekutizionetserozozidzaayendabwanjimwabata.

Katswiri pa ndale Ernest Thindwawatim’masiku 100 oyambirira a utsogoleriwaMutharikaAmalawiaonambwadza.

Iyewatikwanthawiyoyambachiyambireniulamulirowazipanizambiri, AmalawiaonakugawanamitundundipoPulezidentiangoyang’anira.

“Ngakhalemlanduukadalikukhoti, Mutharikandimtsogolerimpakakhotilidzagamulemwanjiraina. AkadakhalawinaakadagwiritsantchitomphamvuzakekulunzitsaAmalawindipoanthuakadamukonda,” wateroThindwa.

Iyewatikutikulunzanitsakokutheke, Mutharika, ndunazabomakomansoatsogoleri a zipanizotsutsabomaakuyenerakusankhamawuolankhula pa misonkhano.

Ndipokadaulo pa pakayendetsedwekazinthum’dzikoMakhumboMunthaliwatiboma la Mutharikalisadzilimbitsemtimakutizinthuzilibwinopomwezayipiratu.

“M’dzikomulizipolowezokhazokha, anthuakuotcherananyumba, galimotongakhalensomaofesindiyen’kumatizilibwino? Ayi,” wateroMunthali.

Iyewatingatiboma la Mutharikalikufunaanthualikhulupilire, liwapangirezomweakufuna.

Komandunayofalitsankhaniyomwensoimalankhuliraboma Mark BotomaniwatiMutharikawayendamofewa.

“Sitikuonapochipsinjochilichonse. Mutharikawayendetsabwinodzikondipoakukwaniritsazomweadalonjeza,” wateroBotomani.

Iyewatim’masiku 100 apitawa, boma la Mutharikalabzala kale zitukukomongamisewu, damu la madzikuDedza, kuonjezeramphamvuzaasilikalipowagulirasitimazankhondokomansokusainiramaubaleaukazembeosiyanasiyana.

“Amenesakufunaakhale, komaMutharikawatiuzakutiakufunachitukukopaliponsendipoifendunazaketikupangachitukukochomwakathithi,” wateroBotomani.

Amalawiakufunamkuluwabungwe la Malawi Electoral Commission (MEC) Jane Ansahatulepansiudindokomapolankhulandiwayilesiya BBC, MutharikaadamenyetsankhwangwapamwalakutiAnsahsachoka pa pandowo.

Share This Post