Chichewa
-
‘Auka’ atatha zaka 11 m’manda ku ntchisi
Pa 16 April 2005 lidali tsiku lachisoni m’mudzi mwa Ngwanje, T/A Malenga m’boma la Ntchisi pomwe mayi Nkomanyama Charles…
Read More » -
Bwalo lilanga mphunzitsi wochimwitsa mwana
Bwalo la milandu la majisitireti la Mzuzu lapeza mphunzitsi wina wolakwa pamlandu wochimwitsa mtsikana wosakwana zaka 16, komanso kupereka…
Read More » -
Anatchezera
Amandikakamirabe Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 19 zakubadwa, vuto langa ndi lakuti pali mnyamata wina wake amene amandifuna koma ineyo…
Read More » -
‘Tinkapita kumpira wa Silver’
Ena akangomva za masewero ampira amalingalira zogenda, kuvala ziyangoyango kapena kuimba nyimbo basi komatu monga zochitika zina zilizonse, iyi…
Read More » -
Ndaziona: Aona kuwala ku Mozambiki
Mwezi wathawu osewera awiri, Ndaziona Chatsalira ndi Green Harawa adachoka ku Silver Strikers ulendo ku Mozambique kukasaka moyo wina. Chatsalira…
Read More » -
Kamuleni ndi Polisi Palibe
Tsikulo nkhani idavuta ndi ya anyamata ena aja adabutsa bwalo la milandu m’taunimu. Adaganiza bwanji anthuwa? Uku nkugenda kupolisi wamkulu…
Read More » -
Adzikhweza pamkangano wa madzi osamba ku Nkhatabay
Chisoni chakuta banja lina ku Bula, T/A M’bwana, m’boma la Nkhata Bay pomwe mnyamata wa Sitandade 8 wadzimangirira atayambana…
Read More » -
Zikavuta, nawo anthu amakoka ngolo
Ngolo imakokedwa ndi ng’ombe kapena abulu, koma pena zikavuta nawo anthu amakoka. Pachithunzipa, anyamatawa adakoka ngoloyi ng’ombe zitathawa. Nanga titani?…
Read More » -
Amukwenya ponena olumala kuti ‘agalu’
Banja lina lapempha mkulu woyang’anira za maphunziro m’maboma a Phalombe, Mulanje ndi Thyolo (Divisional Education Manager—DEM) kuti athane ndi…
Read More » -
Apalamula poitana T/A kumwambo pafoni
Mwambo wobzala mitengo ku Bula m’boma la Nkhata Bay udasokonekera Lachinayi pamene mfumu yaikulu M’bwana idakana kupita kumwambowu ati kaamba…
Read More » -
Aphungu asaiwale kukambirana za njala
Pomwe kwangotsala masiku 9 kuti aphungu a ku Nyumba ya Malamulo akakumane kukambirana za momwe ndondomeko ya chuma yayendera pa…
Read More » -
Dizilo Petulo Palibe, polisi
Nthawi imeneyo nkuti tikudikira Moya Pete kuti atiuze njala athana nayo bwanji pano pa Wenela. Tonse tidaungana poawailesi kuti…
Read More » -
Anatchezera
Akumandiipitsa Zikomo agogo, Ndili ndi chibwenzi ndipo makolo akudziwa ngakhale kuti ndi mwamphekesera chabe. Nthawi ina bambo ake (osati…
Read More » -
Zokhudza mikangano ya ufumu
Nkhani za ufumu zakhala zikuvuta kwa nthawi yaitali. Zina mwa nkhani zomwe zakhala zikupanga mitu ndi mikangano ya ufumu…
Read More » -
Kudali ku sitolo ya ‘Peoples’
Khalidwe la Gift Simkonda lokonda kukagula katundu kusitolo ya Peoples kwa Magalasi ku Ndirande mumzinda wa Blantyre m’chaka…
Read More » -
Galu kusaka mbuyake
Nkhani ya agogo anayi amene adaphedwa ku Neno kaamba koganiziridwa kuti adapha munthu m’matsenga idakhudza Amalawi ambiri. Zoona, ngakhale mkulu…
Read More » -
ANATCHEZERA
Sapereka chithandizo Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 21 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Amuna anga adandisiya ataona kuti ndili ndi…
Read More » -
Aotcha mwana chifukwa cha mkute
Pamene nkhani za njala zikuyala nthenje, mayi wina ku Neno wa zaka 28 zakubadwa waotcha mwana wake m’manja chifukwa…
Read More » -
Mfumu yoba mopusitsa igamulidwa mawa
Bwalo lamilandu la majisitileti ku Ntchisi mawa likuyembekezeka kupereka chigamulo kwa mfumu ina Lachisanu idaepezeka yolakwa pamlandu wakuti inkabera…
Read More » -
Konzani mavuto a kayidi, litero khoti
Khoti la First Grade Magistrate m’boma la Dowa, lalangiza boma kuti likonze ena mwa mavuto omwe akayidi akukumana nawo m’ndende…
Read More »