Chichewa
-
Ulendo womaliza wa Grace Chinga
Thupi la Grace Chinga yemwe adamwalira Lachitatu usiku liikidwa lero m’manda a HHI mumzinda wa Blantyre. Thupi la Grace limayembekezeka…
Read More » -
Woganiziridwa kuba khanda anjatidwa ku Mzuzu
Mayi wina zake zada mumzinda wa Mzuzu atamugwira ataba khanda la psuu la mnzake pachipatala chachikulu cha Mzuzu sabata…
Read More » -
Kodi Idrissa Walesi akutani mu Mozambique?
Mu 2012 ku Mighty Wanderers kudatchuka wosewera wa kumbuyo, Idrissa ‘baba’ Walesi. Atangotchuka, Walesi adasowa ndipo zidamveka kuti wakwawira…
Read More » -
Mowe Pati: Amuna ndi dothi
Tsikulo, mkulu wina adati tipite m’tauni tikaone umo zikukhalira chifukwa mikangano ya oitanira basi komanso oyang’anira mzinda ikukhala bwanji. Tidafika…
Read More » -
Dovu lakula ku nsanje
Anthu ena m’boma la Nsanje alephera kupirira nkhuli ndipo akuphabe ndi kugulitsa nyama ya ng’ombe, mbuzi, nkhumba ndi nkhosa…
Read More » -
Anatchezera
Ndazunguzika Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 18 ndipo ndinazunguzika mutu chaka chatha pomwe ndinapezeka ndi kachilombo ka HIVkoma sindinagonepo ndi…
Read More » -
‘Kudali ku Presbyterian Church of Malawi’
Kudali kuphwanya mafupa ku Dream Centre Assemblies of God mumzinda wa Blantyre Loweruka pa 2 May pamene Faith Mussa amachititsa…
Read More » -
‘Palibe angamange mvula, siyani kuzunza anthu’
Masiku apitawa anthu 7 adawagwira ku Chiradzulu ndipo adawazunza powaganizira kuti akumanga mvula. Adawakolezera moto masanasana kuti aothe ndipo akuti…
Read More » -
Msika wa fodya utsekulidwa April
Misika yaikulu ya fodya m’dziko muno ikhoza kutsekulidwa sabata yachiwiri ya mwezi wa mawa, atero akuluakulu a bungwe lowona…
Read More » -
‘Omanga mvula’ awaothetsa moto likuswa mtengo’
Kudali gwiragwira Loweruka lapitalo m’midzi ya Kazembe, Golosi ndi Ntamba kwa T/A Nkalo m’boma la Chiradzulu pamene anthu olusa…
Read More » -
Za Jessica Bwira ndi zina
Mvula idagwa tsikulo pa Wenela si ndiyo. Kaya inkachokera kuti kaya! Abale anzanga, musandifunse za Jessica Bwira, Mwano Mkangama…
Read More » -
Adatengera Lucky Dube: Liwonde Chibwe
Oimba akubadwirabadwira m’dziko muno. Mmodzi mwa oimba omwe adza ndi mkokomo ndi MacDonald Liwonde Chibwe wa ku Mponela m’boma la…
Read More » -
‘Amatsutsanabe zamakumanidwe awo’
Ambiri akapezana nkukondana nkugwirizana za banja amakhala ndi chikumbumtima cha komwe ndi mmene adakumanirana, koma ndi nkhani yochititsa chidwi…
Read More » -
Wonyozedwa ali moyo Alemekezedwa atamwalira
Gogo wina ku Ntcheu, yemwe amagona pachisakasa chonga pogulitsira tomato abale ake akukana kuti agone m’nyumba yabwino, adalemekezedwa atamwalira…
Read More » -
Zaka 18 kwa mphunzitsi wochimwitsa mwana
Mphunzitsi yemwe adachimwitsa mtsikana wasukulu wa zaka zosadutsa 16 komanso kumupatsa mankhwala ochotsera pathupi wapukusa mutu wopanda nyanga bwalo…
Read More » -
Anatchezera
Sakuyankhanso foni Zikomo, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndidapeza bwenzi langa mu 2012. Poyamba ankalimbikira kuti andikwatire chaka chomwecho…
Read More » -
Chimanga chikololedwa chochepa—Unduna
Kauniuni woyamba wa zokolola wasonyeza kuti chaka chino Amalawi akolola chimanga chocheperako kusiyana ndi chaka chatha, chikalata chimene unduna wa…
Read More » -
‘Apolisi adalakwa pomanga aphungu’
Katswiri wina wa za malamulo ndi anthu ena othirapo ndemanga agwirizana ndi bungwe la Malawi Law Society (MLS) ponena kuti…
Read More » -
Into women’s world
With the fashion industry booming, there is a higher demand for models. And over the last few years Malawi has…
Read More » -
Mulibe Sisters ali kuti?
Tikamalira, muzitimvera Tikamalira, musamakwiye Mudziwe ndife ana anu Sindikudziwa kuti nyimbo ya Lucius Banda idabwera bwanji m’mutu mwanga. Ndipo sindikudziwa…
Read More »