Chichewa
-
Kucheza ndi Ibu Mphanje: Gaba wochemerera Bullets
Anthu otsata masewero a mpira wa miyendo alipo ambiri koma ena amaonjeza kukonda kwake. Ena adachita kufika popereka maina achilendo…
Read More » -
Anatchezera: Akukana kunditsata
Agogo, Ndine mnyamata wa zaka 20 ndipo ndili pachibwenzi ndi mtsikana wa zaka 22 ndipo timakondana kwambiri koma vuto ndi…
Read More » -
Tidakumana Bwanji: ‘Padali pagalaja ku Area 25’
Garage ndi malo okonzera galimoto, koma ukachita mphumi malowa uthanso kudya nawo bwino monga momwe Mike Tembo adachitira. Iyetu adasodzerapo…
Read More » -
Aletsa zionetsero ku Nkhata Bay
Gulu la anthu omwe amakonza zionetsero zofuna kukakamiza boma kuti likonze msewu waukulu wopita ku Mzuzu, limange msika komanso malo…
Read More » -
Amanga wometa mnzake kumanyazi
Zachilendo akuti zachitika ku Mangochi komwe apolisi amanga mkulu wina pomuganizira kuti adameta mnyamata wa fomu 4 malo aulemu. Mneneri…
Read More » -
Escom ikhazikitsa ntchito yatsopano ya magetsi
Boma kudzera ku bungwe la magetsi la Electricity Supply Corporation of Malawi (Escom) lakhazikitsa pulojekiti yotchedwa ‘Ndawala’ yobweretsa magetsi kumidzi…
Read More » -
APM akuzemba PAC —Akatswiri a ndale
Othirira ndemanga pa ndale m’dziko muno ati zimene mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika wachita posakumana ndi a bungwe la…
Read More » -
Lekani kulozanalozana, nyengo yasintha—MET
Nthambi yoona za kusintha kwa nyengo ya Malawi Meteorological Services (MET) yati anthu adziwe kuti nyengo ikusintha ndipo aleke kulozana…
Read More » -
Oferedwa akusowa mtendere ku ntchisi
Adanena mawu oti mvula ikakuona litsiro sikata sadaname. Banja la anamfedwa ena ku Ntchisi likusowa mtendere pamene nyakwawa ya m’mudzi…
Read More » -
‘Youth Week’ ibwereredi —Achinyamata, mafumu
Mtsogoleri wa achinyamata pa ndale wa bungwe la Young Politicians Union Clement Mukuwa wati ndi wosangalala ndi ganizo la…
Read More » -
anatchezera
Amandimenya Zikomo gogo, Ndine mtsikana wa zaka 20 ndipo ndili pachibwenzi ndi mwamuna wa zaka 25. Tili ndi mwana mmodzi…
Read More » -
Agwiririra ndi kupha gogo
Pomwe dziko lapansi likukumbukira tsiku la amayi pamutu woti ‘Kuthetsa Nkhanza kwa Amayi ndi Ana’, anthu achiwembu ku Mchinji…
Read More » -
Wotsatsa msuweni wake Amangidwa miyezi iwiri
Ngati bodza, koma apolisi m’boma la Nkhotakota atsimikiza kuti bwalo la milandu la majisitireti lagamula kuti Bakali Chirwa, wa…
Read More » -
Joyce Mhango: Nyale ya zisudzo
Azisudzo m’Malawi muno akhala akulimbika kutukula lusoli koma chifukwa cha zovuta zina ndi zina mwayi woonekera nkulandira mphotho pa zochita…
Read More » -
Zaka 14 kaamba kovulaza mkazi wake
Juliyasi Dalasoni wa m’mudzi mwa Zidana, T/A Phambala m’boma la Ntcheu, amulamula kupita kundende kukagwira ukaidi kwa zaka 14…
Read More » -
‘Mnzanga ndiye adandipezera’
Sylvester Namiwa, mneneri wa pulezidenti Peter Mutharika lero ndi wokondwa kwambiri kuti ukadaulo wa mtolankhani wa Nation, Albert Sharra,…
Read More » -
Gule wa utse ku Nsanje
Mtundu ulionse umakhala ndi zinthu zokumbikira mtundu wawo kapena chikhalidwe. Umu zilinso choncho ndi mtundu wa Asena ku Nsanje komwe…
Read More » -
Boma lilonga mafumu 250
Boma kudzera muunduna wa za maboma aang’ono latsimikiza kuti mafumu 250 aikidwa pamndandanda wolandira nawo mswahara kupangitsa kuti ndalama zopita…
Read More » -
Ulendo womaliza wa Grace Chinga
Thupi la Grace Chinga yemwe adamwalira Lachitatu usiku liikidwa lero m’manda a HHI mumzinda wa Blantyre. Thupi la Grace limayembekezeka…
Read More » -
Woganiziridwa kuba khanda anjatidwa ku Mzuzu
Mayi wina zake zada mumzinda wa Mzuzu atamugwira ataba khanda la psuu la mnzake pachipatala chachikulu cha Mzuzu sabata…
Read More »