Chichewa
-
Miyambo ya ukwati
Ukwati sangotengana ngati nkhuku, pali miyambo yake. Ukalakwitsa miyamboyi, mavuto ena akakugwera umasowa mtengo wogwira. Pakati pa Achewa miyambo ya…
Read More » -
Miyezi ikutha osalandirandalama za mthandizi
Akugona ndi njala, ena akudya nyanya (mizu ya mitengo yoyanga) pamene akudikirirabe ndalama zawo za ntchito ya mthandizi yomwe…
Read More » -
Afuna chitukuko chofanana m’madera a aphungu
Ntchito za chitukuko m’madera oyimiriridwa ndi aphungu a ku Nyumba ya Malamulo chiyamba kufanana tsopano ntchito yodulanso malire ikachitika.…
Read More » -
Apolisi akwidzinga anthu 10 ku Neno
Akuwaganizira kuti adatengapo mbali kupha agogo anayi Apolisi m’boma la Neno Lachinayi adanjata anthu 10 powaganizira kuti adatengapo mbali pa…
Read More » -
‘Padali pachiwaya cha tchipisi’
“Adayezetsa tchipisi cha K150, ine ndidamuonjezera kuti agule cha K200.” Mmenemo ndi momwe zidayambira kuti Henry Mbinga akumane ndi Chimwemwe…
Read More » -
Chigodola chavuta ku Nsanje
Ng’ombe 70 m’boma la Nsanje zikutsalima, pamene 65 000 kumeneko zili pachiopsezo chotenga matenda a chigodola amene abonga m’bomalo.…
Read More » -
TCC imema alimi a fodya kulembetsa
Bungwe loyang’anira za malonda a fodya m’dziko muno la Tobacco Control Commission (TCC) lati alimi a fodya omwe sadalembetse…
Read More » -
Tisiyanitse kukongola ndi kuphweka
Amayi ndi atsikana ambiri tikafunsiridwa ndi munthu wokwatira, timakwera mumtengo, kumva bwino kuti ngakhale uja ali ndi mkazi wake waponyabe…
Read More » -
Ulimi wamthirira usangokhala nyimbo
Mkonzi, Ndimamva chisoni njala ikamagwa m’dziko muno chifukwa choti mwagwa chilala pamene tili ndi nyanja ndi mitsinje yambiri yomwe simaphwera…
Read More » -
Chilala chavuta maboma ambiri
Nduna ya zamalimidwe ndi chitukuko cha madzi, Dr Allan Chiyembekeza, wati pakhala msonkhano wounikira momwe ng’amba yakhudzira anthu makamaka m’chigawo…
Read More » -
Ngakhale ng’amba ikuwaula mmera, akuchilimikabe
Nkhani ya ng’amba siyochita kufunsa chifukwa momwe zikuwaukira mbewu m’minda ndiumboni wakuti dzuwa lalanda malo a mvula. Alimi ambiri…
Read More » -
Obzala nthawi ya maliro athothedwa
Thambo likagwa m’mudzi, aliyense amayenera ayandikire chifupi ndi siwa kuti athandizane nthawi ya zolemetsayi. Kudagwa zovuta m’mudzi mwa Mazale kwa…
Read More » -
Ndinkacheza ndi mchimwene wake
Akuti amapitapita kunyumba kwa namwali potengera chinzake chomwe chidalipo pakati pa iye ndi mchimwene wa namwaliyo. Emmanuel Katiko akuti…
Read More » -
Kuphana kwaphweka pa Wenela
Tsiku limenelo diraiva wina adati ndikhale kondakitala wa ganyu paulendo wake wolowera ku Machinjiri. Nkhani zinkakamba anthu mmenemo zidali zachilendo…
Read More » -
Mkazi wansanje achekacheka mnzake
Bwalo la milandu la majisitireti ku Mchinji masiku apitawa lidalamula kuti mayi wansanje amene adachekacheka mayi mnzake ndi mpeni…
Read More » -
Mlatho uwu si uli ku Mwanza
Munthu atakutenga ku Blantyre usiku, kukumanga kumaso nkukakusiya pamlatho uwu, ukhoza kuyesa uli ku Mwanza utawerenga chikwangwani ichi. Nkhawa tsopano…
Read More » -
Zampira zenizeni ndi CJ Banda
John CJ Banda ndi kaputeni wa Blue Eagles, komanso ndi katundu wofunika ku Flames. Iye wapeza mwayi wokasewera ku…
Read More » -
Anatchezera
Sakundilipira Zikomo gogo, Ndakhala ndikugwira ntchito kukampani ya alonda ina kwa miyezi 11 popanda masiku opuma. Mwezi ulionse amatidula K500…
Read More » -
Atuma anthu kupha
Apolisi m’boma la Chitipa atsekera m’chitokosi bambo wina pomuganizira kuti adatuma achiwembu kupha mkazi wake wakale. Facksoni Simbeye adatuma Filisoni…
Read More » -
Njala ikhaulitsa a Malawi
…Ma Admarc ena kuli gwagwagwa! Zafika pena. Ngati wina samwalira ndi njala ungokhala mwayi chabe koma zinthu zaipa m’dziko muno…
Read More »