Chichewa
-
Anatchezera
Sakuthandiza mwana Agogo, Ndine mtsikana wa zaka 19 ndipo ndili ndi mwana mmodzi. Ndidali pabanja koma litatha bambowo samatumiza chithandizo…
Read More » -
Mayi amwalira kokafuna golide
Mayi wa zaka 36 wamwalira ku Salima pamene dothi la mumtapo wa golide yemwe amafunafuna litamugwera iye ndi mwamuna…
Read More » -
Dyson Gonthi: Msangalatsi wa pakanthawi
Kwa amene tidabadwa pakanthawi Dyson Gonthi ndilo dzina limayambirira kubwera mumtima tikamva ting’oma ndi kanyimbo ka Nzeru Nkupangwa komanso ambiri…
Read More » -
‘Zidayambira m’malingaliro’
Mwina tinganene kuti kulimbikira ntchito ndiko kudapangitsa kuti malingaliro omwe Steve Chimenya wa ku Zomba adali nawo asanduke zenizeni…
Read More » -
Adzinjata Kaamba Ka Mkazi Wamwini
Chisoni chidaphetsa nkhwali. Ku Masasa, mumzinda wa Mzuzu mnyamata yemwe adalembedwa ntchito ya zomangamanga pakhomo pa bambo wina m’derali…
Read More » -
Chisamakome mbuzi kugunda galu
Kawirikawiri tikamva za nkhanza zozungulira chuma cha masiye, timaganizira kuvutidwa kwa amayi ndi ana m’manja mwa abale a mwamuna yemwe…
Read More » -
Flames itenga mwezi ikukonzekera Guinea
Timu ya mpira ya dziko lino ya Flames itenga mwezi umodzi ikukonzekera masewero ake ndi Guinea omwe adzachitike mwezi…
Read More » -
Akapeza thanthwe pokumba manda zimatha bwanji?
Zochitika kumanda nzambiri nthawi yokumba manda koma palibe nthawi yomwe adzukulu amakhaula kwambiri kuposa pamene apeza thanthwe dzenjelo lisadathe…
Read More » -
Kanthu n’khama: Alimi akuchita kuthirira fodya
Kudula kwa mvula kutionetsa zachilendo mpaka alimi kuchita kuthirira m’minda ya fodya kuti mwina angaphulepo kena kake. Alimi ochenjera akuyesetsa…
Read More » -
Boma lapempha amalawi adekhe pa za mathanyula
Boma lapempha aMalawi kuti adekhe pankhani yoimitsa lamulo loletsa umathanyula m’dziko muno. Polankhulapo mkati mwa sabatayi, mneneri wa boma…
Read More » -
Chitamponi kanthu pa za fisp
Wapampando wa komiti ya zaulimi m’Nyumba ya Malamulo, Felix Jumbe, wati boma lichitepo kanthu pa za mmene ndondomeko ya…
Read More » -
Alimbana ndi ntchemberezandonda ku Zomba
Unduna wa zamalimidwe wati ntchemberezandonda zomwe zabuka m’boma la Zomba zisatayitse anthu mtima chifukwa akatswiri apita kale m’madera omwe akhudzidwa…
Read More » -
Alosera mvula kugwa mochuluka
Nthambi yoona za nyengo ya Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) yati mvula yamphamvu ikhala ikugwa kwa…
Read More » -
Chaka ndi miyezi inayi ali m’chipatala osaimirira
Maloto a Alineti Molosi wa zaka 15 odzakhala namwino akhoza kufera m’mazira ngati madotolo sakwanitsa kumuchiza nthenda yozizira miyendo…
Read More » -
Anatchezera
Sitinakumanepo Anatchereza, Ndili ndi mkazi amene ndidamufunsira pafoni koma sitinaonanepo. Timangoimbirana foni basi koma amandiuza kuti amandikonda kwambiri. Ndimukhululupirire? …
Read More » -
Za maukwati, mabanja
Money is gooooood Musayense njerego, awa ndi mawu ochokera munyimbo ya Miracle Money ya mnyamata wodziwa kuimba nyimbo zauzimu, Onesmus.…
Read More » -
Zaka zinayi kwa ofuna kuba alubino
Njonda ziwiri zochokera m’boma la Mzimba Lachitatu zidagamulidwa kukasewenza jere kwa zaka zinayi ndi kugwira ntchito yakalavula gaga chifukwa chofuna…
Read More » -
Katsoka: Mtsogoleri wa alakatuli
Ulakatuli ndi limodzi mwa maluso omwe akuphukira kumene m’dziko muno. Zaka zambiri zapitazo, anthu samatenga ndakatulo ngati njira yofalitsira…
Read More » -
Adzikonzera ‘mpumulo wa bata’
Ukayenda umaona agalu a michombo ndithu. Ku Rumphi aliko oyenda masanasana pamene bambo wina wa zaka 62 wakumbiratu manda…
Read More » -
‘Mwayi kuthima kwa magetsi’
Pomwe ena akudandaula za kuthimathima kwa magetsi, ena akusimba lokoma kuti adapatirapo mwayi wabanja. Victor Mpunga yemwe pa 28…
Read More »